Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

July 8, 2005

Mmene Mungapezere Ntchito ndi Kukhalitsa Pantchitopo

Masiku ano vuto la ulova lakula kwambiri chifukwa ntchito zikusowa zedi. Kodi mungatani kuti mupeze ntchito ndi kukhalitsa pantchitopo?

3 Kukhala Lova Mwadzidzidzi

4 Mfundo Zisanu Zomwe Zingakuthandizeni Kupeza Ntchito

10 Zimene Mungachite Kuti Mukhalitse Pantchito

14 Ndinafunitsitsa Kukwanitsa Cholinga Changa

16 Mbiri ya Mawotchi a Pamkono

19 Kodi Kuba M’masitolo Ndi Nkhani Yaikulu Bwanji?

20 N’chifukwa Chiyani Anthu Amaba M’masitolo?

22 Kodi Ndani Amavutika Chifukwa cha Kuba M’masitolo?

25 Mmene Munthu Angasiyire Kuba M’masitolo

27 Ndinkafuna Kuchidziwa Bwino Chipembedzo Changa’

28 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .

Kodi Ndingachite Zotani Ngati Mtsikana Akundifuna?

31 “Pa Chilankhulo Chathu Palibe Mawu Otukwana”

32 Dziwani Zimene Baibulo Limaphunzitsa

Kodi Muyenera Kuopa Armagedo? 12

Pali zinthu zambiri zomwe anthu amakhulupirira zokhudza Armagedo zomwe si zoona. Kodi Armagedo yotchulidwa m’Baibulo muyenera kuiona bwanji?