Zamkatimu
Zamkatimu
September 8, 2005
Mgwirizano ndi Wofunika Kwambiri pa Moyo
Kodi mgwirizano umene umaoneka m’chilengedwe ungakhale ukutisonyeza za mgwirizano womwe udzakhalepo Ufumu wa Mulungu ukamadzalamulira?
3 Kufunika kwa Mgwirizano M’chilengedwe
5 Chifukwa Chake Mgwirizano Uli Wofunika Kwambiri
11 Padziko Lonse Padzakhala Mgwirizano
13 Zimene Achinyamata Amadzifunsa
Kodi Ndingatani Kuti Ndisayambe Kucheza ndi Anthu Olakwika?
18 Mulungu Amalemekezeka Tikamachita Zinthu Moona Mtima
19 “Ntchito Imene Anthu Ambiri Amagwira Padziko Lonse”
23 Tsogolo la Ntchito Zokopa Alendo
26 Achinyamata Amene Amalalikira Mogwira Mtima
28 Tinapeza Chinachake Chabwino Koposa
32 Kodi Mulungu Amatisamaliradi?
Kodi Kupemphera kwa Mariya Virigo N’koyenera? 16
Anthu mamiliyoni ambiri amapemphera kwa Mariya. Kodi zimenezi
[Chithunzi pachikuto]
Pachikuto: Mbalame yofiira mlomo yakwera pamsana pa njati. Mbalameyi imadya tizilombo tomwe tili pa thupi la njatiyo, ndiponso imalira pochenjeza njatiyo ngati kukubwera choopsa
[Chithunzi patsamba 2]
Anamgumi okhala ndi linunda pamsana amathandizana ntchito kuti apeze chakudya
[Mawu a Chithunzi]
© Brandon Cole