Mlozera Nkhani wa Voliyumu 86 ya Galamukani!
Mlozera Nkhani wa Voliyumu 86 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Anthu Ena Akandiuza Mavuto Awo, 2/8
Kucheza ndi Anthu Olakwika, 8/8, 9/8
Kucheza ndi Anthu pa Intaneti, 10/8, 11/8
Kupeza Chibwenzi pa Intaneti, 5/8, 6/8
Ndingatani Kuti Ndiziugwira Mtima? 3/8
Ndingatani Mnyamata Amene Ndimamufuna Akandikana? 1/8
Ndingatani Ngati Mtsikana Akundifuna? 7/8
Ndizigwira Ntchito Yamanja Chifukwa Chiyani? 4/8
Tichite Kukhala ndi Mwambo Wonse wa Ukwati? 12/8
CHIPEMBEDZO
Kodi Yesu Kristu Ndi Mulungu? 5/8
CHUMA NDI NTCHITO
Kupeza ndi Kukhalitsa Pantchito, 7/8
MAUNANSI A ANTHU
Amayi Ndi Aphunzitsi, 3/8
Kukongola Kofunika Kwambiri, 1/8
Kumvetsa Mavuto Amene Dokotala Wanu Akukumana Nawo, 2/8
Kuthandiza Achinyamata Amene Ali Pamavuto, 4/8
MAYIKO NDI ANTHU
Chigwa cha Ngorongoro (Tanzania), 1/8
Malo Ovuta Kuwamvetsa a ku Africa, 11/08
“Ndinu Dr. Livingstone, Eti?” (Tanzania), 2/8
Nyanja ya Pinki (Senegal), 10/8
“Palibe Mawu Otukwana” (mtundu wa Apache), 7/8
“Tikakumane Pachitsime” (Moldova), 11/8
MBONI ZA YEHOVA
Achinyamata Amalalikira Mogwira Mtima, 9/8
Kupereka Umboni Wabwino ku Sukulu (Mexico), 10/8
Kusintha Akaidi, 4/8
Mulungu Amalemekezeka Tikamachita Zinthu Moona Mtima, 9/8
“Muzinyadira Zimenezi,” 6/8
Ndende za ku Mexico, 10/8
“Ndikanakonda Anthu Akanadziwa Zimenezi!” (Dominican Republic), 1/8
Nkhani Yakale Inakhudza Mitima ya Anthu, 8/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Kukopeka ndi Mlengi Chifukwa cha Kukongola kwa Choonadi (T. Fujii), 8/8
Kwalembedwa Kuti Ndidzawaonanso (R. Phillips), 1/8
Ndinafunitsitsa Kukwanitsa Cholinga Changa (M. Serna), 7/8
Ndinatha Kutumikira Mulungu Ngakhale Zinali Zovuta (I. Mikitkov), 5/8
Nkhondo Imene Inasintha Moyo Wanga (M. Molina), 11/8
Sayansi ndi Baibulo Zinandithandiza Kudziwa Cholinga cha Moyo (B. Oelschlägel), 12/8
Tinapeza Chinachake Chabwino Koposa (F. Del Rosario de Páez), 9/8
Wokonzeka Kuthandiza Ena (C. Vavy), 3/8
Zilema Zanga Sizinandifooketse (K. N’Guessan), 12/8
SAYANSI
Dzuwa Kuwala Pakati pa Usiku, 6/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Khansa Yapakhungu, 6/8
Kuchita Zinthu Zolimbitsa Thupi, 6/8
Kumvetsa Mavuto Amene Dokotala Wanu Akukumana Nawo, 2/8
Kumwa Mowa Mopitirira Muyeso, 10/8
Moyo Wopanikizika, 2/8
Utsi Wakupha (wa nkhuni), 6/8
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Kodi Akazi Azibisa Kukongola Kwawo? 10/8
Kodi Baibulo Limapondereza Akazi? 11/8
Kodi Kufatsa N’kupanda Mphamvu? 1/8
Kodi Kufuna Kutchuka N’kulakwa? 6/8
Kodi Mulungu Ali Paliponse? 3/8
Kodi Mulungu Amakondera Mitundu Ina ya Anthu? 12/8
Kodi Muyenera Kuopa Armagedo? 7/8
Kodi Nyenyezi Zingakuthandizeni Kudziwa Tsogolo Lanu? 8/8
Kugwiritsa Ntchito Zithunzi Popemphera, 5/8
Kupatsa Ana Chisamaliro Chimene Amafunikira, 2/8
Kupemphera kwa Mariya Virigo? 9/8
Maukwati a Amuna Okhaokha Kapena Akazi Okhaokha, 4/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Mgwirizano, 9/8
Tomato, 3/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Dziko Likusakazidwa Kwabasi, 1/8
Kuba M’masitolo, 7/8
Kudyetsa Anthu Wani Biliyoni, 8/8
Kukhala Mopanda Mantha, 8/8
Kupezera Chakudya Anthu Okhala M’mizinda, 12/8
Kusowa Pokhala, 12/8
Mafilimu, 5/8
Masoka Achilengedwe, 8/8
Mmene Mungapindulire ndi Manyuzipepala, 11/8
Msampha wa Kumwa Mowa Mopitirira Muyeso, 10/8
Njira Zosawononga Dziko Zopangira Magetsi, 3/8
Ntchito Zokopa Alendo, 9/8
Vuto la Padziko Lonse la Kusowa kwa Nyumba, 10/8
Zimene Osauka Angayembekezere, 11/8
ZOSIYANASIYANA
Mafoni a M’manja Ndi Abwino Kapena Ndi Oipa? 2/8
Mapiri Ndi Ofunika kwa Zamoyo, 4/8
Mumayendetsa Galimoto Mbali Iti ya Msewu? 4/8
Pakhomo Paukhondo, 6/8