Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Mungayankhe Bwanji?

ZINACHITIKIRA KUTI?

1. Kodi zomwe zili pachithunzipa zinachitikira m’nyanja iti?

Lembani mzera kuzungulira yankho lanu pa mapupa.

Nyanja Yaikulu

Nyanja ya Galileya

Mtsinje wa Yordano

Nyanja ya Mchere

◆ Kodi mungatchule mayina a anthu awiri omwe sali m’bwatowo?

․․․․․

․․․․․

◆ N’chifukwa chiyani ndi munthu mmodzi yekha amene akumira?

․․․․․

ZINACHITIKA LITI?

Lembani mzera kuchokera pa chithunzi kufika pa deti lolondola.

1077 B.C.E. 947 B.C.E. 647 B.C.E. 539 B.C.E. 537 B.C.E.

2. Danieli 5:5

3. Yeremiya 1:1-3

4. 2 Samueli 2:1-4

KODI NDINE NDANI?

5. Ndinakantha Afilisti 600 ndi mtoso wa ng’ombe.

KODI NDINE NDANI?

6. Ndinaswa lumbiro la atate wanga podya uchi.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo lembani mavesi kapena vesi la m’Baibulo lomwe likusowapo.

Tsamba 7 N’chifukwa chiyani anthu amafa? (Aroma  6:․․․)

Tsamba 9 Kodi Baibulo limalonjeza tsogolo lotani? (Chivumbulutso 21:․․․)

Tsamba 12 Kodi n’chiyani chingachititse munthu kuchita zinthu mosaganizira bwino? (Mlaliki 7:․․․)

Tsamba 19 Kodi n’kuti kumene tingapeze malangizo otitsogolera, ndipo n’chifukwa chiyani tingawapeze kumeneko? (2 Timoteo  3:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali patsamba 14)

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Nyanja ya Galileya.​—Yohane 6:1, 16.

◆ Yesu ndi Petro.​—Mateyu 14:26-31.

◆ Petro anakayikira; Yesu sanakayikire.​—Mateyu 14:31.

2. 539 B.C.E.

3. 647 B.C.E.

4. 1077 B.C.E.

5. Samagara.​—Oweruza 3:31.

6. Jonatani.​—1 Samueli 14:27.

[Mawu a Chithunzi patsamba 31]

Top circle: U.S. Fish & Wildlife Service, Washington, D.C./Duane C. Anderson