Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

January 2006

Kodi M’tsogolo Muli Zotani?

Kodi munayamba mwaganizirapo kuti dzikoli lidzakhala lotani zaka 10, 20, kapena kuposerapo m’tsogolomu? Baibulo limapereka zifukwa zogwira mtima zotithandiza kukhulupirira kuti m’tsogolomu tidzasangalala kwambiri kuposa kale lonse.

3 Kwa Owerenga

5 Kodi Tili ndi Tsogolo Labwino?

6 Kodi Dzikoli Likulowera Kuti?

13 Nkhungu Imathandiza Komanso Imawononga

16 Basi Adutsa!

18 Zimene Baibulo Limanena

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kudalira Baibulo Kuti Lizititsogolera?

20 Zochitika Padzikoli

21 Michael Agricola “Anasintha Zinthu Kwambiri”

24 Maselo Ofiira a M’magazi Ndi Odabwitsa Kwambiri

30 Kuchokera kwa Owerenga

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Mwana Akamwalira

N’chifukwa Chiyani Ndimadzivulaza? 10

Werengani za anthu amene akuvutika chifukwa chodzivulaza, chizolowezi chomwe chimatchedwanso kudzicheka, ndipo werenganinso zifukwa zimene amachitira zimenezi.

Chikhulupiriro Chandithandiza Kupirira Matenda Oopsa 25

Werengani nkhani ya mnyamata wina amene wakhala moyo wosangalala ndiponso waphindu, ngakhale kuti ali ndi matenda amene anam’pheratu ziwalo.