Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Mungayankhe Bwanji?

KODI ZINACHITIKA KUTI?

1. Kodi chozizwitsa chomwe achisonyeza panochi chinachitika pafupi ndi mzinda uti?

Lembani mzere kuzunguliza yankho lanu pa mapupa.

Nazarete

Zafoni

Adamu

Yeriko

◆ Kodi Eliya anakwera “kumwamba” kwake kuti?

․․․․․

◆ N’chifukwa chiyani Elisa anapempha magawo awiri a mzimu wa Eliya?

․․․․․

Kambiranani: Kodi zomwe anapempha Elisazi zikukuphunzitsani chiyani?

ZINACHITIKA LITI?

Lembani mzere kuchokera pa chithunzi kufika pa deti lolondola.

29 C.E. 30 31 32 33 36

2. Luka 3:1, 2

3. Yohane 5:1-9

4. Yohane 2:13; 3:1-21

NDINE NDANI?

5. Mwamuna wanga analamula kuti ndiphedwe, koma malangizo a mwana wa bambo anga aakulu anandipulumutsa.

NDINE NDANI?

6. Ndinapita ku kachisi ndisanakwanitse chaka chimodzi ndipo sindinachokeko kwa zaka sikisi zotsatira.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowekapo.

Tsamba 5 Kodi mungachititse munthu wina kukukondani? (Nyimbo ya Solomo 8:․․․)

Tsamba 6 Kodi chikondi chenicheni chimakhala chotani? (Akolose 3:․․․)

Tsamba 13 Kodi Yesu anatsimikizidwa panthawi iti kuti ndi Mwana wa Mulungu m’njira yapadera ndiponso yamphamvu kwambiri? (Aroma 1:․․․)

Tsamba 27 Kodi ndi mavuto otani amene amabwera chifukwa chongotsatira chilakolako chathu osadziletsa? (Aroma 1:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali pa tsamba 20)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Yeriko.—2 Mafumu 2:4-11.

◆ Mumlengalenga.—Nsanja ya Olonda, 8/1/05 tsa. 9.

◆ Zikuoneka kuti ankafuna magawo awiri ngati amene ankapatsidwa kwa mwana wamwamuna woyamba kubadwa.—Nsanja ya Olonda, 11/1/03 tsa. 31.

2. 29 C.E.Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalako, * mutu 11.

3. 31 C.E.Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalako, mutu 29.

4. 30 C.E.Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalako, mutu 17.

5. Estere.—Estere 2:7, 17; 3:12, 13; 4:12-17; 8:3-8.

6. Yoasi.—2 Mbiri 22:11, 12; 23:20–24:1.

[Mawu a M’munsi]

^ ndime 37 Lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.

[Mawu a Chithunzi patsamba 31]

Top circle: Courtesy of London Ambulance Service NHS Trust; third circle from top: Courtesy of Tourism Queensland