Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

March 2006

Kodi Chikondi Chapita Kuti?

Masiku ano, anthu ambiri amaona kuti sakondedwa. Komabe, chikondi n’chofunika kwambiri kuti tizisangalala ndiponso kuti tizikhala ndi moyo wabwino. Phunzirani mmene mungakhalire ndi khalidwe lapadera limeneli.

3 Kufuna kukondedwa

4 Chifukwa Chake Chikondi Chenicheni N’chovuta Kupeza

8 Mmene Mungapezere Chikondi Chenicheni

10 Kulandira Mafoni Angozi ku London

12 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Yesu Analidi Mwana wa Mulungu?

18 Nthanga Imene Inazungulira Dziko

24 Ulendo Wokaona Nkhosa Zam’tchire

26 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

Kodi Ndingapewe Bwanji Zogonana Kusukulu?

29 Zochitika Padzikoli

30 Kuchokera kwa Owerenga

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Tsiku Lofunika Kwambiri M’mbiri Yonse ya Anthu

Chilumba Chokongola Kwambiri cha Mchenga 14

Bwerani nafe pamene tikupita kukaona chilumba chokongola ku dera lofunda kum’mwera kwa matanthwe a m’nyanja opangidwa ndi zamoyo zing’onozing’ono otchedwa Great Barrier Reef ku Australia

‘Ndikufuna Kutumikira Mulungu Ndisanafe’ 21

Pamene Mamie anali ndi zaka 12, anathawa kwawo nyumba yawo ikuyaka moto pankhondo yapachiweniweni. Anawombedwa ndi chipolopolo ndipo anthu ankaganiza kuti amwalira. Werengani nkhani yake yokhudza mtima.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

Courtesy of Tourism Queensland