Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

May 2006

Kodi Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wautali Bwanji?

Kodi n’chiyani chimayambitsa kukalamba? Kodi pali chilichonse chomwe anthu angachite kuti akuthetse?

3 Kodi Mungapewe Kukalamba?

4 N’chifukwa Chiyani Timakalamba?

7 Kodi Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wautali Bwanji?

14 Zochitika Padzikoli

18 Michael Servetus Anafufuza Choonadi Yekhayekha

22 Masiponji ndi Zamoyo Zoderereka Koma Zochititsa Chidwi

25 Munda Wokongola Mogometsa

28 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Kukhala Munthu Wamtendere N’kothandiza?

30 Kuchokera kwa Owerenga

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 “Ndikufuna Ndizingoliwerengabe”

Thandizani Mwana Wanu Wamkazi Kukonzekera Kutha Msinkhu 10

Kodi mungayambe liti kulankhula ndi mwana wanu wamkazi za kusamba? Kodi nkhaniyi mungaiyambe bwanji?

Ndiziwerenga Chifukwa Chiyani? 15

Imvani zomwe achinyamata ochokera m’mayiko 11 ananena atafunsidwa za mmene kuwerenga kumavutira ndi ubwino wa kuwerenga.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

DNA: Photo: www.comstock.com