Zamkatimu
Zamkatimu
July 2006
Mmene Mungakhalire ndi Banja Losanga lala
Masiku ano pali zinthu zambiri zimene zikutekesa mabanja. Onani mmene mungalimbitsire banja lanu potsatira mfundo zabwino komanso zothandiza kuti banja lonse likhale losangalala.
3 Kodi Banja Lingapirire Mavuto Aakulu?
6 Mmene Mungakhalire ndi Banja Losangalala
10 Uthenga Uyenera Kuperekedwa
16 N’chifukwa Chiyani Madzi a M’nyanja Zikuluzikulu Amakhala Amchere?
22 Kodi Kusisita Mwana N’kofunika?
23 Zimene Achinyamata Amadzifunsa
Kodi Ndidzagwire Ntchito Yotani Pamoyo Wanga?
32 Kodi N’zotheka Kuti Banja Likhale Losangalala?
Ndinali Wotaya Mtima Koma Tsopano Ndine Wosangalala 11
Mnyamata wina anakonza zodzipha chifukwa chodziimba mlandu ndiponso kuthedwa nzeru. Imvani mmene Mawu a Mulungu anam’thandizira kukhala ndi mtendere weniweni wa mumtima.
‘Katswiri wa ku Britain Yemwe Anaiwalika’ 26
Katswiriyu anali ndi moyo m’nthawi ya Isaac Newton, ndipo anali mmodzi mwa akatswiri a ku Britain amene anatulukira kapangidwe ka zinthu zosiyanasiyana. Koma m’mbuyomu sanali kutchulidwa kawirikawiri m’mabuku a mbiri yakale. Onani zomwe zinachititsa.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Images courtesy of the Posner Memorial Collection, Carnegie Mellon University Libraries