Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

September 2006

Magazini Yapadera

Kodi Mlengi Alipo?

Kodi n’zomveka kukhulupirira kuti kuli Mlengi chifukwa cha kupangidwa mwaluso kwa zinthu zamoyo?

Kodi Muyenera Kukhulupirira Ndani? 3

Kodi Zamoyo Zimatiphunzitsa Chiyani? 4

Kodi Mulungu Anagwiritsa Ntchito Chisinthiko Polenga Zamoyo? 9

Kukambirana ndi Katswiri wa Sayansi 11

Pulofesa wina wa sayansi ya zimene zimachitika m’kati mwa zinthu zamoyo akufotokoza maganizo ake pa nkhani ya chisinthiko.

Kodi Chisinthiko Chinachitikadi? 13

Kodi kusintha kwa maselo a zamoyo kapena kupulumuka kwa zamoyo zamphamvu zokhazokha kumayambitsa mitundu yatsopano ya zamoyo?

Kodi Sayansi Imatsutsana ndi Nkhani ya mu Genesis? 18

Kodi Baibulo limaphunzitsadi kuti zinthu zonse zinalengedwa m’masiku sikisi enieni a maola 24?

Chifukwa Chimene Timakhulupirira Kuti Kuli Mlengi 21

Asayansi ndi ochita kafukufuku ena akufotokoza zifukwa zawo.

Dongosolo Lodabwitsa la Zomera 24

Kodi zomera zimapanga mizere yozungulirazungulira pokula, mwangozi chabe?

Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Ndimakhulupirira Zokhudza Chilengedwe? 26

Onani mmene wachinyamata angafotokozere zikhulupiriro zake kusukulu.

Kodi Zimene Mumakhulupirira Zili ndi Ntchito? 29

Onani mmene zimakhudzira moyo wanu wonse.

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Kodi Mulungu Amatisamaliradi?

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

Dinosaur: © Pat Canova/​Index Stock Imagery