Kodi Mungayankhe Bwanji?
Kodi Mungayankhe Bwanji?
TCHULANI ZOLENGEDWA ZAUZIMUZI
Lembani mzere kulumikiza mtundu wa mngelo ndi chithunzi chogwirizana naye, kenaka yankhani funsolo.
Mkulu wa angelo
Kodi mkulu wa angeloyu amadziwika ndi dzina loti chiyani?
Akerubi
Kodi akerubi ankalondera chiyani mu Edene?
Aserafi
Kodi Yesaya anamva aserafi akunena chiyani?
Angelo
Kodi angelo onse pamodzi alipo osachepera angati?
1. ․․․․․
2. ․․․․․
3. ․․․․․
4. ․․․․․
▪ Kambiranani: Kodi kudziwa za banja la Yehova lakumwamba kungakuthandizeni bwanji kulimba mtima?—2 Mafumu 6:15-17.
ZINACHITIKA LITI?
Lembani mzere wolumikiza chochitika chilichonse ku chaka chomwe chinachitikira.
1761 B.C.E. Cha m’ma538 B.C.E. 33 C.E.
1728 B.C.E. Cha M’ma455 B.C.E. 44 C.E.
7. Danieli 6:22
NDINE NDANI?
8. Sindinamvere machenjezo a mngelo ndi kulira kwa bulu.
NDINE NDANI?
9. Ndinapereka uthenga kwa Danieli, Zekariya, ndi kwa mayi a Emanueli.
KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowekapo.
Tsamba 3 Kodi kuonera TV kukufanana bwanji ndi kudya uchi? (Miyambo 25:․․․)
Tsamba 7 N’chifukwa chiyani tiyenera kusamala n’zimene timaonera pa TV? (Miyambo 13:․․․)
Tsamba 11 Kodi munthu akafa maganizo ake amatani? (Salmo 146:․․․)
Tsamba 21 Kodi Yehova amaona bwanji achinyamata amene ali ndi matenda ovutika kudya? (Salmo 22:․․․)
Zithunzi Zoti Ana Apeze
Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.
(Mayankho ali patsamba 27)
MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
1. Akerubi. “Njira ya ku mtengo wa moyo.”—Genesis 3:24.
2. Mkulu wa angelo. Mikayeli.—Yuda 9.
3. Angelo. Mamiliyoni ambiri.—Danieli 7:10.
4. Aserafi. “Woyera, Woyera, Woyera, Yehova.”—Yesaya 6:3, 6, 7.
5. 44 C.E.
6. 1761 B.C.E.
7. Cha m’ma 538 B.C.E.
8. Balamu.
9. Gabrieli.
[Mawu a Chithunzi patsamba 31]
Middle circle: ©Alan Copson/Agency Jon Arnold Images/age fotostock