Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

October 2006

Kodi TV Imakhudza Bwanji Moyo Wanu?

TV mwina ndi chinthu chimene chimakhudza maganizo ndi zochita za anthu mwamphamvu kwambiri kuposa china chilichonse. Kodi inuyo imakukhudzani bwanji?

3 Kodi TV Imakuberani Nthawi?

4 TV Ndi “Mphunzitsi Wakabisira”

8 Njira Zothandiza Kuti Musamaonere TV Kwambiri

10 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Mungathe Kuthandiza Anthu Akufa?

12 Dzitetezeni Kuti Asakubereni Galimoto!

15 Mlatho wa Tower Bridge ndi Njira Yolowera mu London

27 Chifukwa Chimene Sindikondwerera Halowini

28 Kuchokera kwa Owerenga

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Kuthandiza Mtsikana Wovutika Maganizo

Kodi Ndili ndi Matenda Ovutika Kudya? 18

Matenda otchedwa anorexia, bulimia, ndi kudya kwambiri, akuvutitsa moyo ndi thanzi la anthu mamiliyoni ambiri, achinyamata ndi achikulire omwe. Kodi tingalimbane bwanji ndi matenda amenewa?

Anthu Otchedwa Aromani—Zaka 1,000 za Chimwemwe ndi Chisoni 22

Aromani akhalapo kwa zaka mahandiredi ambiri, ndipo amadziwikanso ndi maina ena akuti Majipise, Matsigoina, Maketano, ndi ena ambiri. Kodi anachokera kuti? Kodi amafuna kuti moyo wawo wa m’tsogolo udzakhale wotani?