Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

November 2006

Kuyankha Funso Lovuta Kwambiri Loti “Chifukwa Chiyani?”

Anthu ambiri akukumana ndi masoka achilengedwe, uchigawenga, kapena ngozi zazikulu. Kodi inuyo munayamba mwafunsapo kuti n’chifukwa chiyani Mulungu akulola zinthu zimenezi kuchitika? Werengani nkhaniyi kuti mupeze yankho lake, komanso chitonthozo ndi chiyembekezo chopezeka m’Baibulo.

3 Funso Lovuta Kwambiri

5 N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika?

9 Mulungu Amatiganizira!

10 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

Kodi Ndingathetse Bwanji Chizolowezi Chimenechi?

15 Baibulo la M’chinenero Chamakono

20 Dziwani Zambiri za Mtsinje Waukulu wa Mekong

26 “Nthawi ya Chakudya Imatithandiza Kuti Tizikondana”

27 Ndinapulumutsidwa ku Masautso Anga Onse

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 “N’labwino Kwambiri”

Zamoyo za ku Chigwa Chotchedwa Death Valley 22

Werengani za malo otentha kwambiri padziko lonse, ndipo onani mmene zamoyo zambirimbiri zochititsa chidwi zikusangalalira kumeneko.

Kodi Ngati Anthu Akukondana Ndiye Kuti Palibe Cholakwika Atagonana Asanakwatirane? 13

Kodi ndi bwino kuti anthu omwe ali pachikondi koma sanakwatirane azigonana? Kodi chimenecho ndicho chikondi chenicheni? Kodi Mulungu amaliona motani khalidwe limeneli? Werengani nkhaniyi kuti mupeze mayankho omveka bwino a m’Baibulo.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

COVER: Flood: © Tim A. Hetherington/​Panos Pictures

PRAKASH SINGH/​AFP/​Getty Images