Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

December 2006

Kodi Yesu Anali Ndani?

Kodi anthu olemba mbiri amati Yesu ndi wofunika motani? N’chifukwa chiyani iye ali wosiyana ndi anthu ena onse? Nanga n’chifukwa chiyani zimenezo ziyenera kukhala zofunika kwa ife?

3 Munthu Woposa Onse Amene Anakhalapo

4 Chifukwa Chake Iye Ali Wofunika Kwambiri

7 Moyo Umene Adzabweretse

10 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

N’chifukwa Chiyani Amandiikira Malamulo Ambirimbiri?

16 “Unabadwa kwa Makolo Oyera Kuposa Onse”

20 “Kodi Mumakondwerera Tsiku la Agogo Aakazi?”

21 Anakonda Zimene Anaphunzira

24 Calypso Nyimbo Zamakolo za ku Trinidad

26 Kodi Tikanatani Pakadapanda Abulu?

28 Kuchokera kwa Owerenga

29 Zochitika Padzikoli

30 Mlozera Nkhani wa Magazini A Galamukani! a 2006

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Mphatso Yamtengo Wapatali

Ndinali Mwana Wolowerera 13

Werengani za mnyamata amene anapandukira makolo ake oopa Mulungu ndiponso zimene zinam’chititsa kuti asinthe moyo wake n’kubwerera.

Kodi Kumwa Mowa N’kulakwa? 18

Baibulo limanena za mavuto amene angabwere chifukwa cha mowa. Choncho, kodi kumwa mowa n’koyenera?