Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

January 2007

Matenda Onse Adzatha!

Sayansi yapititsa patsogolo kwambiri ntchito zachipatala ndiponso zolimbana ndi matenda. Komabe, anthu akupitiriza kuvutika ndi matenda. Kodi idzafika nthawi imene matenda onse adzathe?

3 Aliyense Akufuna Moyo Wathanzi!

4 Kodi Sayansi Idzathetsa Matenda Onse?

10 Matenda Onse Adzatha!

12 Mfumu Imene Inafunafuna Nzeru

15 Zochitika Padzikoli

16 Taonani Bwenzi la Alimi—Chikumbu

18 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Chikhristu Chalephera Kusintha Zinthu?

23 Malo a Zachilengedwe a Belize Barrier Reef—Chuma Chadziko Lonse

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Kutonthoza Amene Akulira

Chingalawa cha Nowa Chinapangidwa Mwaluso 20

Katswiri wolemba mapulani a kapangidwe ka sitima zapamadzi watulukira kuti chingalawa cha Nowa chinapangidwa mogwirizana kwambiri ndi mapulani amakono a kapangidwe ka sitima.

Kodi Ndingayambe Chibwenzi Nditafika Msinkhu Wotani? 27

Kodi ndinu wokonzeka kuyamba chibwenzi? Taonani mfundo zitatu zimene zingakuthandizeni kuyankha funso limeneli.