Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

March 2007

Kuthandiza Achinyamata Masiku Ano Kupeza Zomwe Amafunikira

Achinyamata ambiri amagwiritsira ntchito Intaneti pouza ena zakukhosi kwawo ndiponso pofunafuna anthu oti azicheza nawo. Taonani njira yabwino imene ingawathandize kupeza zofunikirazi.

3 Achinyamata Avuta ndi Intaneti!

4 Kuthandiza Achinyamata Kukhalabe Okhulupirika

8 Thandizani Achinyamata Kupeza Zomwe Amafunikira

13 Ndinasankha Ntchito Yabwino Kwambiri

16 Chilumba cha Kamchatka ku Russia N’chochititsa Kaso

20 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Kudzichepetsa ndi Mantha Kapena N’chamuna?

22 Zochitika Padzikoli

23 “Nzeru Zam’chilengedwe”

30 Kachilombo Kopirira Modabwitsa

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

31 Mwambo Wosafunika Kuuphonya

Mungathe Kuphunzira Chinenero China! 10

Kuphunzira chinenero china ndi ntchito yovuta. Onani mmene anthu ena akwanitsira kuchita ntchito imeneyi mosangalala.

Bwanji Ngati Wina Atandifunsira Kuti Tikagonane? 26

Kwa achinyamata ena kugonana kwafika pongokhala ngati kudya ndi kumwa. Onani mmene mungalimbanirane ndi chizolowezi choopsa chimenechi ndi kupewa mavuto aakulu.