Zamkatimu
Zamkatimu
October 2007
Magazini Yapadera
Kodi Tiyenera Kukhulupirira Baibulo?
Palibe buku lina lililonse limene lafalitsidwa kwambiri kuposa Baibulo. Koma kodi tingadziwe bwanji kuti uthenga wa m’Baibulo ndi wochokera kwa Mulungu? Onani m’magaziniyi umboni, monga woperekedwa ndi mbiri yakale ndiponso sayansi, womwe ungakuthandizeni kuyankha funsoli.
5 Chifukwa Chake Tiyenera Kukhulupirira Baibulo
1. Ndi Lolondola Pankhani za Mbiri Yakale
2. Olemba Ake Ananena Zoona Zokhazokha
4. Ndi Lolondola Pankhani za Sayansi
Ngati Baibulo linalembedwa ndi anthu, kodi lingakhale bwanji Mawu a Mulungu?
12 Baibulo Lakumana ndi Zambiri
Onani mavuto amene Baibulo ladutsa, mpaka kukhala buku lotchuka kwambiri padziko lonse.
15 Zinthu Zakale Zimasonyeza Kuti Baibulo Ndi Lolondola
Werengani za zinthu zakale zochititsa chidwi zimene zimapereka umboni woti Baibulo ndi lolondola.
19 Kodi Baibulo Limanena za Chiyani?
M’Baibulo muli mfundo yaikulu imodzi. Kodi mukuidziwa?
Werengani za zikhulupiriro zopeka zisanu zokhudza Baibulo zimene anthu ambiri ali nazo.
23 Kodi Muyenera Kukhulupirira Malangizo a M’Baibulo?
Onani mmene Baibulo lingakuthandizireni kukhala ndi moyo wabwino ndi wosangalala.
26 Zimene Achinyamata Amadzifunsa . . .
Ndizitsatira Mfundo za M’Baibulo Chifukwa Chiyani?
Onani chimene chimachititsa achinyamata ambiri kuona kuti malangizo a m’Baibulo ndi ofunika kwambiri.
29 Baibulo Ndi Umboni Wosatha wa Chikondi cha Mulungu
Sikuti Baibulo langokhala buku labwino. Onani chifukwa chake.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
© The Trustees of the Chester Beatty Library, Dublin
Musée du Louvre, Paris