Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Pankhani ya Zimene Zimachitika Munthu Akafa—Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Pankhani ya Zimene Zimachitika Munthu Akafa—Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Pankhani ya Zimene Zimachitika Munthu Akafa—Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Siliphunzitsa zimene anthu ambiri akhala akuuzidwa. Mwachitsanzo siliphunzitsa kuti . . .

▪ Anthu onse abwino amapita kumwamba.

▪ Achibale amene anafa tiziwalambira.

▪ Akufa angathe kutivulaza kapena kutithandiza.

▪ Anthu ali ndi chinachake chimene sichifa. Chiphunzitsochi chimapezeka m’zipembedzo zambiri ndipo ndicho maziko a ziphunzitso zambiri zomwe si zam’malemba, monga zakuti kuli moto kumwamba ndiponso kuti anthu akafa amakabadwanso kwinakwake kapena amakauka chinthu chinachake.

Koma zimene Baibulo limaphunzitsa n’zolimbikitsa komanso n’zotsitsimula kwambiri. Buku limene mukuliona panoli lafotokoza zimenezi m’njira yosavuta kumva. Mukhoza kuitanitsa bukuli polemba zofunika m’mizere ili m’munsiyi ndipo tumizani ku adiresi imene ili pomwepoyo kapena ku adiresi yoyenera imene ili patsamba 5 la magazini ino.

□ Ndikupempha kuti munditumizire buku limene lasonyezedwa panoli.

□ Nditumizireni munthu kuti ayambe kuchita nane phunziro la Baibulo lapanyumba laulere.