Zamkatimu
Zamkatimu
July 2008
Kodi mungatani kuti banja lanu liziyenda bwino?
Mabanja ambiri nthawi zina amayenda bwino, koma nthawi zina amakumana ndi zovuta. Ndiye kodi mungatani kuti banja lanu likhale losangalala ndi lolimba? Baibulo lili ndi mfundo zothandiza kwambiri pankhaniyi.
4 N’chiyani Chimayambitsa Mavutowo?
6 Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino
12 Kodi Dzikoli Lidzakhalabe ndi Zinthu Zokwanira Anthu Onse?
19 Zimene Achinyamata Amadzifunsa
Kodi Ndingatani Kuti Kulambira Mulungu Kuzindisangalatsa?
24 Tizigoba Tokongola ta ku Niihau
26 M’kamwa
32 “Bukuli Ndi Labwino Kwambiri!”
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kupewa Zamizimu? 10
Anthu ambiri amachita zinthu zokhulupirira mizimu chifukwa cha chidwi basi. Koma kodi kuopsa kwake n’kotani? Kodi Mulungu amaiona bwanji nkhani yokhulupirira mizimu?
Ngalande za ku Britain Zikuchititsabe Chidwi 13
Ngalande zimenezi zinakumbidwa m’ma 1800, ndipo kenako anasiya kuzigwiritsa ntchito. Panopa azikonzanso moti zikukopa alendo ambiri okaona malo.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Courtesy of British Waterways