Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2008

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2008

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2008

CHIPEMBEDZO

Amene Ali Kumanda Adzakhalenso ndi Moyo, 9/08

Kodi Pali Chipembedzo Choona Chimodzi Chokha? 3/08

Kubwera kwa Matchalitchi ku Tahiti, 8/08

Masiku Otsiriza, 4/08

N’chifukwa Chiyani Tili ndi Moyo? 12/08

MAUNANSI A ANTHU

Kodi Ana Anu Mumawadziwa Bwino? 6/08

Kuchitira Nkhanza Akazi, 1/08

“Kukonda Kwambiri Anthu” (Russia), 8/08

Ngati Mwana Wanu Amagwiritsa Ntchito Intaneti, 10/08

Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino, 7/08

MAYIKO NDI ANTHU

Akasupe a Madzi Otentha (Hungary), 3/08

Anthu a ku Okinawa Amakhala ndi Moyo Zaka Zambiri, 11/08

Anyani Odabwitsa a M’matanthwe (Gibraltar), 3/08

Chakudya cha ku Thailand, 7/08

Chilumba Chachikulu (Hawaii), 3/08

Inatenga Zaka Zoposa 120 (Australia), 2/08

Kamudzi ka Asodzi Kanasintha N’kukhala Mzinda Waukulu (Tokyo, Japan), 1/08

Kanyanja Kokongola Kwambiri (Gulf of California), 5/08

Kubwera kwa Matchalitchi ku Tahiti, 8/08

‘Kulowa pa Diso la Singano’ (Bass Strait, Australia), 11/08

Kumene Mtsinje Umayenda Cham’mbuyo (Cambodia), 10/08

Kuyenda pa Boti ku Kerala (India), 4/08

Miyambo Yakale Ilipobe ku Mexico, 3/08

Mlatho Umene Unali Kumangidwa Mobwerezabwereza (Bulgaria), 1/08

Mtundu wa Anthu Umene Unatenga Malo ku Asia (Mongol), 5/08

Ngalande za ku Britain, 7/08

Nyama Zakuthengo Zimasangalala (Gabon), 1/08

Nyanja Yakufa (Israel), 1/08

Nyengo Imene Dzuwa Silituluka (mayiko a ku Arctic), 12/08

Puerto Rico, 10/08

Sitima Yopanda Mateyala (China), 11/08

Tizigoba Tokongola ta ku Niihau (Hawaii), 7/08

“Tsiku Limene Kunada Masana” (Africa), 3/08

Zidole Zochita Zisudzo (Austria), 1/08

Zithunzi Zokongola Kwambiri Zamiyala (Italy), 12/08

MBIRI YA MOYO WA ANTHU

Kulalikira Uthenga Wabwino ku Madera Akutali (H. Jones), 3/08

Kumene Ndinamvera Dzina Loti Yehova (P. Kovár), 6/08

Mmene Moyo Unalili Zinthu Zitasintha (C. Park), 12/08

Mulungu Anandithandiza Kugonjetsa Mayesero (V. Asanov), 9/08

Ndinali Mkulu wa Asilikali Koma Tsopano Ndine “Msilikali wa Khristu (M. Lewis), 2/08

MBONI ZA YEHOVA

Anachira ndi “Buku Lakale Kwambiri” (buku la Nkhani za Baibulo), 12/08

Aphunzitsi Ake Analiyamikira (buku la Mafunso Achichepere Akufunsa), 10/08

“Bukuli Ndi Labwino Kwambiri!” (buku la Chimwemwe cha banja), 7/08

Chikondi Champhamvu Kuposa Mphepo Yamkuntho! 8/08

Galamukani! Inamuthandiza 9/08

Msonkhano wa Chigawo Wakuti “Mzimu wa Mulungu Umatitsogolera,” 5/08, 6/08

“Sindinkadziwa Kuti Mulungu Ali ndi Dzina” (buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani), 9/08

SAYANSI

Diso la Njuchi (tizilombo), 3/08

Dziko lapansi Likutentha, 8/08

Kangaude, 1/08

Kodi Mipukutu Yakale Inalembedwa Liti? 2/08

Maloboti, 9/08

Mapazi a Nalimata, 4/08

M’kamwa, 7/08

Mmene Chikodzera Chimadzitetezera, 12/08

Mmene Gulugufe Amadziwira Komwe Akupita, 11/08

Mwendo wa Mbalame, 9/08

Nthaka (kudalirana), 8/08

Sitima Yopanda Mateyala, 11/08

“Tsiku Limene Kunada Masana” (kadamsana), 3/08

UMOYO NDI MANKHWALA

Anthu a ku Okinawa Amakhala ndi Moyo Zaka Zambiri, 11/08

Kuunika M’thupi−M’malo Mopanga Opaleshoni, 11/08

Magazi Akayezedwa Kachilombo ka HIV, 6/08

Matenda a Asperger, 9/08

Nyengo Imene Dzuwa Silituluka (kudwala chifukwa cha nyengo), 12/08

Salankhula Koma Timamvana (Rett syndrome), 10/08

Vuto Lokhala Alubino, 7/08

ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA

Kodi Ndikaulule Tchimo la Mnzanga? 12/08

Kodi Ndingatani Kuti Kulambira Mulungu Kuzindisangalatsa? 7/08

Kodi Ndingatani Kuti Mapemphero Anga Azikhala Abwino? 11/08

Kodi Ndingatani Kuti Ndisagonje Poyesedwa?, 8/08

Kodi Ndingatani Ngati Mbale Wanga Wadzipha, 6/08

Kodi Ndingodzipha? 5/08

Kupanikizika Kusukulu, 9/08

Kutukwana, 3/08

Masewera a Pakompyuta? 1/08

N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Sandikhulupirira? 4/08

Ngati Ndili ndi Matenda Aakulu Kapena Chilema? 2/08

Nthawi Yofikira Panyumba, 10/08

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kodi Dzikoli Lidzakhala Paradaiso? 5/08

Kodi Mulungu Amafuna Kuti Muzichita Chiyani? 4/08

Kodi Mulungu Amakhululuka Machimo Akuluakulu? 2/08

Kodi Mulungu Ndi Wotani? 10/08

Kodi Ndi Bwino Kumenyana ndi Wachiwembu? 6/08

Kodi Yesu Anabadwa Liti? 12/08

Kukhala Mutu Wabanja, 1/08

Mafano, 8/08

Mayina Aulemu, 9/08

Zamizimu, 7/08

Zikhulupiriro za Makolo, 3/08

Zinthu Zothandiza Popemphera, 11/08

ZINYAMA NDI ZOMERA

Akambuku a ku Siberia, 6/08

Anyani Odabwitsa a M’matanthwe (Gibraltar), 3/08

Chimanga, 8/08

Chulu cha Chiswe, 6/08

Diso la Njuchi (tizilombo), 3/08

Kadziweni Kanyama Aka, 7/08

Kangaude, 1/08

Kodi Umenewu Ndi Mtengodi? (malambe [boab]), 5/08

Kukhala Bwinobwino M’chipale Chofewa, 2/08

Mafuta a Golide a ku Mediterranean (mafuta a Maolive), 4/08

Mapazi a Nalimata, 4/08

Mitengo Yam’madzi (malunje), 6/08

Mmene Chikodzera Chimadzitetezera, 12/08

Mmene Gulugufe Amadziwira Komwe Akupita, 11/08

Mmero Wodutsira Mkaka (mwana wa ng’ombe), 10/08

Mwana wa Nyani Atalira, 8/08

Mwendo wa Mbalame, 9/08

Njati za ku Ulaya, 10/08

Nthaka (kudalirana), 8/08

Nyama Zakuthengo Zimasangalala (Gabon), 1/08

Paua (nkhono), 12/08

ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE

Anthu Ambiri Akuopa Zam’tsogolo? 5/08

Dziko lapansi Likutentha, 8/08

Kodi Dzikoli Lidzakhalabe ndi Zinthu Zokwanira Anthu Onse? 7/08

Kodi Mphatso Zachifundo Zingathetse Mavuto? 5/08

Kodi Zachiwawa Zingathetsedwe? 2/08

N’chifukwa Chiyani Nsomba Zikusowa? (kupha nsomba mosakaza), 11/08

ZOSIYANASIYANA

Chinyengo cha Otsatsa Malonda, 12/08

Kodi Mungatani Kuti Zinthu Zizikuyenderani? 11/08

Kuimba Mwaluso, 4/08

Nyimbo ndi Mphatso ya Mulungu Yotitsitsimula, 5/08

Oona za Ndege Amakutetezani, 4/08

Zidole Zina Si Zongoseweretsa (zidole), 6/08