Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsiku Loyenera Kulikumbukira

Tsiku Loyenera Kulikumbukira

Tsiku Loyenera Kulikumbukira

Chonde Mudzakhale Nafe—Lachinayi pa April 9, 2009

Usiku woti aphedwa mawa, Yesu Khristu anayambitsa mwambo wokumbukira imfa yake. Pamwambowu, iye anagwiritsa ntchito vinyo ndi mkate wopanda chofufumitsa zomwe zimaimira magazi ndiponso thupi lake lopanda uchimo. Kenako Yesu analamula kuti: “Muzichita zimenezi pondikumbukira ine.”—Luka 22:19.

Ife Mboni za Yehova timamvera lamulo limeneli ndipo tikukupemphani kuti mudzakhale nafe pamwambo umenewu chaka chino. Mungafunse Mboni za Yehova za m’dera lanu kuti mudziwe nthawi yeniyeni ndiponso malo amene kudzachitikire mwambowu.