Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani Wa Magazini a Galamukani! a 2009

Mlozera Nkhani Wa Magazini a Galamukani! a 2009

Mlozera Nkhani Wa Magazini a Galamukani! a 2009

CHIPEMBEDZO

Achinyamata a Katolika Anauzidwa Kuti Azilalikira, 6/09

Dzina la Mulungu ku Denmark, 11/09

Nyenyezi Imene Inatsogolera “Anzeru a Kum’mawa,” 12/09

MAUNANSI A ANTHU

Achinyamata Kodi Mungathane Bwanji ndi Mavuto Anu? 9/09

Ana Ambiri Akumapanikizika, 5/09

Anthufe Ndi Amodzi, 11/09

Kalankhulidwe Kogometsa Koimba Likhweru, 2/09

Kodi Kutha kwa Banja Kumakhudza Bwanji Ana? 10/09

Kodi Tsankho Limayamba Bwanji? 8/09

Kuthandiza Ana Amene Ali Ndi Vuto Lophunzira, 1/09

Mfundo Zothandiza Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino, 10/09

N’zotheka Kulera Nokha Ana, 10/09

Thandizani Ana Anu Kuti Akule Bwino, 6/09

Ubwino Wosonyezana Chikondi, 12/09

MAYIKO NDI ANTHU

Akapolo Oiwalidwa a ku South Pacific, 1/09

Albarracín Ndi Tawuni Yokongola Kwambiri (Spain), 7/09

Anthu Otcheza Mchere ku Sahara, 1/09

“Dera Loiwalika” la ku Bolivia, 11/09

Dzina la Mulungu ku Denmark, 11/09

Galimoto Yopalasa? (Bangladesh), 7/09

Mankhwala Odzikongoletsera Ochokera ku Mitengo (Madagascar), 7/09

Mzinda wa Bucharest(Romania), 4/09

Mzinda wa Plovdiv (Bulgaria), 6/09

Nyama ndi Zomera Zikutha (Spain), 3/09

MBIRI YA MOYO WA ANTHU

Chimene Chinandichititsa Kusiya Kukonda Nkhondo (T. Stubenvoll), 12/09

Ndakhala Wokhulupirika kwa Zaka Zoposa 70 (J. Elias), 9/09

Ndinamasulira Mabuku Mobisa kwa Zaka 30 (O. Mockutė), 6/09

Ndinasiya Usilikali N’kuyamba Kutumikira Yehova (A. Hogg), 11/09

Ndinathawa Nkhondo (S. Tan), 5/09

Sindinabwerere M’mbuyo Ngakhale Kuti Ndili ndi Matenda Olepheretsa Kuwerenga (M. Henborg), 2/09

Tinadalitsidwa Chifukwa Chokonda Kwambiri Mulungu (P. Worou), 3/09

Tinapeza Zimene Tinkafuna (B. Tallman), 1/09

MBONI ZA YEHOVA

Analimba Mtima Kufotokoza Zimene Amakhulupirira, 12/09

‘Chitseko Chimene Yehova Yekha Ndi Amene Angatsegule’ (manda), 8/09

Kabuku Kanga Kapinki (buku la Mphunzitsi Wamkuruyo), 3/09

Kugwiritsitsa Dzanja Lamanja la Mulungu (matenda a pakhungu), 9/09

‘Limayankha Mafunso Athu’ (Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri), 7/09

Mphunzitsi Anasintha Maganizo Ake (Georgia), 3/09

Msonkhano Wachigawo wa “Khalani Maso,” 5/09, 6/09

Wodwala Ali Ndi Ufulu Wosankha, 6/09

Zimene Mukufuna Zili M’Baibulo, 11/09

SAYANSI

Chigoba cha Chikumbu, 5/09

Dzikoli Linapangidwa Kuti Likhale ndi Zamoyo, 2/09

Kachipangizo Kochititsa Chidwi, 3/09

Kodi Mumatha Kusunga Zinthu Zanu Mwachinsinsi? 8/09

Kufika ku Mars, 2/09

Kumwamba Kuli Zinthu Zambiri Zodabwitsa, 8/09

Mapiko a Zamoyo Zouluka, 2/09

Masamba a Kakombo, 4/09

Mlomo wa Mbalame Yotchedwa Toucan, 1/09

Mlomo Wochititsa Chidwi wa Nyama ya M’madzi, 3/09

N’chifukwa Chiyani Mulungu Analenga Zonsezi? 12/09

Nthenga za Kadzidzi, 12/09

N’zotheka Ndithu Kuchepetsa Vuto la Kuiwala, 2/09

Umboni Wosonyeza Kuti Nkhani za M’Baibulo N’zoona, 5/09

Woyamba Kujambula Mapu a Dziko Lonse (Mercator), 4/09

Zigoba za Nkhono Zam’madzi, 8/09

Zipangizo Zamakono, 11/09

UMOYO NDI MANKHWALA

Anthu Ovutika Maganizo, 7/09

Kodi Kukachitika Ngozi Mumadziwitsa Ndani? 4/09

Kodi Mungatani Kuti Mwana Wanu Asanenepe Kwambiri? 3/09

Kuchotsa Mimba, 6/09

Kugwiritsa Ntchito Mankhwala Moyenera, 5/09

Kukhalitsa Padzuwa, 6/09

Matenda a Chithokomiro, 5/09

Mayi Wathanzi Amaberekanso Mwana Wathanzi, 11/09

Samalani ndi Poizoni, 12/09

ZACHUMA NDI NTCHITO

Kodi Ndinu Kapolo wa Ndalama? 3/09

Njinga Yonolera Mipeni, 2/09

ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA

Kodi Ndingatani Kuti Ndidziwane Bwino Ndi Makolo Anga? 10/09

Kodi Ndingatani Kuti Ndimuiwale? 2/09

Kodi Ndingatani Kuti Ndizilankhula Momasuka ndi Makolo Anga? 12/09

Kodi Ndingatani Kuti Ndizipewa Kupsa Mtima? 9/09

Kodi Ndingatani Ngati Kholo Langa Lamwalira? 8/09

Kodi Ndipeze Anzanga Ena Abwino? 3/09

Kodi Ndithetse Chibwenzi? 1/09

Kodi Ndizivala Bwanji? 11/09

N’chifukwa Chiyani Atsikana Amangondikana? 5/09

N’chifukwa Chiyani Ndimaopa Kuuza Ena za Chikhulupiriro Changa? 7/09

Ndingatani Kuti Kuwerenga Baibulo Kuzindisangalatsa? 4/09

Ndingatani Kuti Ndizigwiritsa Ntchito Nthawi Moyenera? 6/09

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kodi Abusa Ndi Apamwamba Kuposa Anthu Ena Mumpingo?

Kodi Anthu Oipa Adzakapsa Kumoto? 9/09

Kodi Kukhulupirika M’banja N’kutani? 4/09

Kodi Kutentha Mtembo N’kulakwa? 3/09

Kodi Mulungu Amafuna Kuti Mukhale Wolemera? 5/09

Kodi Mungathetse Bwanji Njala Yanu Yauzimu? 12/09

Kodi Muyenera Kuopa Anthu Akufa? 6/09

Kodi N’kulakwa Mwamuna ndi Mkazi Kukhalira Limodzi Asanakwatirane? 10/09

Kodi N’zotheka Kukonda Adani Athu? 11/09

Kodi Tikamavutika Ndiye Kuti Mulungu Akutilanga? 1/09

Kodi Tsogolo Lanu Linalembedweratu? 2/09

Kusintha Chipembedzo Chanu N’kulakwa? 7/09

ZINYAMA NDI ZOMERA

Chigoba cha Chikumbu, 5/09

Kanyama Kaulesi, 7/09

Kuphunzitsa Njovu, 4/09

Makolo Ogwirizana, 8/09

Mapiko a Zamoyo Zouluka, 2/09

Masamba a Kakombo, 4/09

Mbalame Zimawomba Makoma Mwangozi, 2/09

Mlomo Wochititsa Chidwi wa Nyama ya M’madzi, 3/09

Njovu Zikuluzikulu Zinkapezeka Paliponse ku Ulaya, 5/09

Nsomba Yochititsa Chidwi, 7/09

Nthenga za Kadzidzi, 12/09

Nyama ndi Zomera Zikutha (Spain), 3/09

Nyama Zikuluzikulu za M’nyanja, 12/09

Mlomo wa Mbalame Yotchedwa Toucan, 1/09

Ulimi Wamakono, 9/09

Zigoba za Nkhono Zam’madzi, 8/09

Zipatso Zofunika Kwambiri, 9/09

Ziwombankhanga Zikuluzikulu, 5/09

ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE

Achinyamata Kodi Mungathane Bwanji ndi Mavuto Anu? 9/09

Kodi Madzi Akutha Padzikoli? 1/09

N’chifukwa Chiyani Anthu Amasankhana? 8/09

N’chiyani Chinayambitsa Nkhondo ya Padziko Lonse? 8/09

Ulimi Wamakono, 9/09

ZOSIYANASIYANA

Herode Anali Katswiri pa Zomangamanga, 9/09

Kamvuluvulu Wapanyanja, 9/09

Luso Lopanga Khofi, 8/09

Mungatani Kuti Muziyendetsa Bwino Galimoto? 7/09

Mungatani Ngati Mumapanikizika ndi Sukulu Ndiponso Zinthu Zina? 4/09

Pizza, 1/09