Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2010
Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2010
CHIPEMBEDZO
Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira (Baibulo), 11/10, 12/10
Kodi Khirisimasi Inayamba Bwanji? 12/10
Kodi Ndi Nzeru Kukhulupirira Mulungu? 2/10
Kulambira Njoka, 3/10
Okhulupirira Kuti Kulibe Mulungu, 11/10
MAUNANSI A ANTHU
Kodi Mungakhulupirire Ndani? 10/10
Kudyera Pamodzi, 1/10
Kusungulumwa, 9/10
Kuthetsa Banja, 2/10
Malangizo Otithandiza Kulamulira Lilime, 11/10
“Mwina Nyimbo Ndi Imene Ingathandize,” 9/10
MAYIKO NDI ANTHU
Anthu a ku Thailand, 5/10
Anthu a mtundu wa Batak (Indonesia), 8/10
Anyani Ochititsa Chidwi a ku Indonesia, 7/10
Chakudya Chotentha Kuntchito (India), 11/10
Chivomezi cha ku Haiti, 12/10
Dzina la Mulungu (tchalitchi cha ku Canada), 7/10
Dzuwa Linafiira Ngati Magazi (Iceland), 2/10
Kufufuza Njira Kumpoto kwa Dziko Lapansi, 10/10
Mabwato (Canada), 5/10
Manda a Pansi pa Nthaka a ku Odessa (Ukraine), 3/10
Mfumukazi Elizabeti I (England), 1/10
Mont Blanc, 4/10
Msika wa ku Africa, 1/10
Mtedza Wokoma wa ku Australia, 11/10
Njanji Yochoka Kunyanja Kukafikanso Kunyanja (Canada), 6/10
Nkhalango ya Amazon, 4/10
Nyumba Zoyenda Nazo za Anthu a ku Asia, 9/10
“Wotchi Yaikulu Kwambiri Padziko Lonse” (Britain), 10/10
Zilumba za Faeroe, 3/10
MBIRI YA MOYO WA ANTHU
Loya Anafufuza Zimene Mboni za Yehova Zimaphunzitsa (L. Civin), 8/10
Mulungu Wanditonthoza (V. Colloy), 12/10
Ndikungoona Kuchedwa Kudzawauza Kuti, “Tonse Tilipo” (A. Austin), 8/10
Ndinakopeka ndi Mboni za Yehova (T. Orosco), 3/10
“Ndinakulira M’banja Losakhulupirira Kuti Kuli Mulungu” (F. Vyskočil), 11/10
Ndinali Msilikali Panopa Ndikutumikira Mulungu (G. Bernhardt), 2/10
Ndinalowa Mpikisano Wabwino Kwambiri (K. Bergman), 9/10
Ndinasankha Ntchito Yabwino (P. Kostadinov), 4/10
Ndinasiya Ntchito ya Ndalama Zambiri (M. Márquez), 6/10
Ngakhale Ndinalumala, Ndine Wosangalalabe (J. Várguez), 5/10
MBONI ZA YEHOVA
Aphunzitsi Amachita Chidwi (Bulgaria), 9/10
‘Buku Lothandiza Kwambiri’ (Mphunzitsi Waluso), 7/10
Chivomezi cha ku Haiti, 12/10
Dzina la Mulungu Likulengezedwabe, 7/10
Galamukani! Inathandiza Mayi Kuti Asachotse Mimba, 2/10
Kabuku Kothandiza Ophunzira Baibulo (‘Onani Dziko Lokoma’), 10/10
“Kuphunzira Baibulo Kukuthandiza Anthu Osamva,” 7/10
‘Kuthetsa Mtima Wodzikonda’ (Gibraltar), 1/10
‘Lekani Kuda Nkhawa’ (India), 1/10
Mayi Wina Ali ndi Ufulu Wolera Ana Ake (Spain), 7/10
Misonkhano Yachigawo ya “Khalanibe pa Ubwenzi ndi Yehova,” 5/10, 6/10
Mukufuna Kukhala Bwenzi la Mulungu? (Mexico), 1/10
Mumadziwa Zotani za Mboni za Yehova? 8/10
“Ndikupempha Kuti Mundithandize” (kabuku ka Munthu Amene Mumakonda Akamwalira), 2/10
“Simunataye Mtima” (mayi wa mwana wolumala), 11/10
NYAMA NDI ZOMERA
Anyani, 4/10
Anyani Ochititsa Chidwi, 7/10
Chakudya cha Tizilombo, 3/10
Chimtengo Chochokera ku Kanthanga, 9/10
Diso la Kadziwotche, 7/10
Diso la Nkhanu, 11/10
Kankhono Kam’madzi, 9/10
Khungu la Shaki, 2/10
Lilime la Mbalame ya Choso, 10/10
Mahatchi Ofatsa, 8/10
Mapiko a Tombolombo, 8/10
Mbalame Zampala, 6/10
‘Mbalame Zouluka Mogometsa,’ 7/10
Mbira Zam’mapiri, 10/10
Mfumu ya Nkhalango, 9/10
Mleme Waung’ono Kwambiri, 2/10
Mlomo wa Nankapakapa, 4/10
Mtedza wa Makadamiya, 11/10
Nankapakapa (mbalame), 2/10
Nsomba za Salimoni, 12/10
Ulimi wa Maluwa, 1/10
Ziphaniphani, 6/10
SAYANSI
Anakwanitsa Zinthu Zimene Zinali Zosatheka, 5/10
Himogulobini, 9/10
Kugunda kwa Mtima, 5/10
Pali Umboni Wasayansi Wotsimikizira Zoti Kulibe Mulungu? 11/10
Panagona Luso! 1/10, 2/10, 4/10, 6/10, 7/10, 8/10
9/10, 10/10, 11/10, 12/10
Zinalipo Kale M’chilengedwe, 3/10
UMOYO NDI MANKHWALA
Chimfine, 6/10
Chipatala Choyendayenda, 3/10
Matenda Amene Anavuta Kwambiri (kolera), 10/10
Matenda Ofooketsa Mafupa, 6/10
Matenda Otupa Chiwindi, 8/10
Mungatani Mutadwala Pokwera Phiri? 7/10
Munthu Angatani Kuti Asiye Kusuta? 5/10
Muzinyadira Khungu Lanu, 5/10
Zimene Mungachite Ngati Mumapanikizika Kwambiri, 6/10
ZACHUMA NDI NTCHITO
Chakudya Chotentha Kuntchito, 11/10
Mumapanikizika ndi Ntchito? 1/10
Ngati Ntchito Yatha Mungasamale Bwanji Ndalama? 7/10
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kodi N’kulakwa Kuchita Zinthu Zina Pandekha? 3/10
Kugonana Tili Pachibwenzi Kungachititse Kuti Tizikondana Kwambiri? 4/10
N’chifukwa Chiyani Anyamata Sandifunsira? 1/10
N’chifukwa Chiyani Ndimangokhalira Kukangana Ndi Makolo Anga? 2/10
N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kusamalira Thanzi Langa? 6/10
Ndingakwanitse Bwanji Zolinga Zanga? 10/10
Ndingakwanitse Kukakhala Pandekha? 7/10
Ndingatani Kuti Ndisamadziderere? 5/10
Ndingatani Kuti Ndisamangokhala Wokhumudwa? 9/10
Ndingatani Kuti Ndizigwirizana Ndi Abale Anga? 8/10
Ndisiye Sukulu? 11/10
Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha, 12/10
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Bwanji Mulungu Osangomuwononga Mdyerekezi? 12/10
Kodi Akazi Ayenera Kukhala Atumiki Mumpingo? 7/10
Kodi Atsogoleri Achipembedzo Ayenera Kulipidwa? 6/10
Kodi Mbali Zonse za Baibulo N’zothandiza? 3/10
Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Chabe? 10/10
Kodi Tiyenera Kupemphera kwa “Oyera”? 11/10
Kodi Ziwanda N’zotani? 8/10
Kugwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru, 5/10
Kutembenuzira Munthu Tsaya Lina, 9/10
N’chiyani Chimachititsa Munthu Kukhala Wabwino Kapena Woipa? 4/10
Tsiku Lachiweruzo, 1/10
Zoyenera Kuchita Mukakhala Pachibwenzi, 2/10
ZOSIYANASIYANA
Chibwibwi, 5/10
Fupa Ndi Lolimba Modabwitsa, 1/10
Kodi Gasi Amachokera Kuti? 11/10
Kodi Nthawi Imakucheperani? 4/10
Mawu Amene Amagwiritsa Ntchito Zikawavuta Panyanja, 10/10
Tiyembekezere Zivomezi Zinanso Zikuluzikulu, 12/10