Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zokuthandizani Kuti Zizikuyenderani ku Sukulu

Zokuthandizani Kuti Zizikuyenderani ku Sukulu

● Kodi ndingatani kuti ndithane ndi mavuto a ku sukulu?

● Kodi ndingatani kuti ndizikhoza?

● Kodi ndingatani ngati mphunzitsi wathu ali wovuta ?

● Kodi ndingatani kuti ndizikwaniritsa zolinga zanga?

Zimenezi ndi zina mwa nkhani zomwe zimapezeka m’buku lakuti, Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri ndi lachingelezi lakuti Questions Young People Ask—Answers That Work, Volume 1.

M’mabuku amenewa mungapezemo malangizo ochokera m’Baibulo okuthandizani pa nkhani zokhudza kucheza ndi anzanu, mmene mumamvera komanso mmene mungamachezere ndi anthu omwe si anyamata kapena atsikana anzanu.