Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zina Zothandiza Mabanja

Mfundo Zina Zothandiza Mabanja

BAIBULO LIMAPEREKA MALANGIZO OTHANDIZA KWAMBIRI kwa anthu okwatirana, makolo komanso kwa achinyamata. Malangizo ake angakuthandizeni kukhala oganiza bwino komanso kusankha bwino zochita.​—Miyambo 1:1-4.

BAIBULO LIMAYANKHANSO MAFUNSO OFUNIKA KWAMBIRI MONGA:

Tikukulimbikitsani kuti mufufuze m’Baibulo mayankho a mafunso amenewa komanso ena. Onerani kavidiyo kakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? popanga sikani kachidindo aka kapena pitani pa www.pr418.com.