GALAMUKANI! Na. 2 2020 | Mayankho a Mafunso 5 Okhudza Kuvutika
Kuphunzira Baibulo kungakutonthozeni pamene mwakumana ndi mavuto.
Zimene Ena Amakhulupirira
Onani zimene zipembedzo zosiyanasiyana zimanena pa nkhani ya chifukwa chake timavutika.
1 Kodi Mulungu ndi Amene Amachititsa Kuti Tizivutika?
Anthu ambiri amasokonezedwa ndi ziphunzitso zabodza zokhudza Mulungu. Kodi zoona zake ndi ziti?
2 Kodi Mavuto Athu Timawachititsa Tokha?
Ngati yankho ndi lakuti inde, ndiye kuti tikhoza kukwanitsa kuchepetsako mavuto athu.
3 N’chifukwa Chiyani Anthu Abwino Amavutika?
Baibulo limatithandiza kudziwa chifukwa chake.
4 Kodi Tinalengedwa Kuti Tizivutika?
Kodi Mulungu amene analenga zinthu zokongola zonsezi, angalenge anthufe kuti tizivutika? Ngati sangatero, ndiye kodi chinalakwika n’chiyani?
5 Kodi Kuvutika Kudzatha?
Baibulo limatifotokozera mmene Mulungu adzathetsere mavuto.
Mungapeze Thandizo
Ngakhale zitaoneka ngati mavuto athu sangathe, pali malangizo odalirika omwe angatithandize.