MFUNDO ZOTHANDIZA AMENE AFEREDWA
Magaziniyi Ili ndi Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa
-
KUVUTIKA MAGANIZO CHIFUKWA CHOFEREDWA
Kodi munthu akaferedwa amakumana ndi mavuto otani? N’chifukwa chiyani anthu amene aferedwa amafunika kuwalimbikitsa?
-
Nkhaniyi ikufotokoza maganizo olakwika omwe anthu ena amakhala nawo komanso zimene zinachitikirapo ena ataferedwa. Ngati inunso muli ndi chisoni chifukwa choferedwa, nkhaniyi ingakuthandizeni kudziwa zimene anthu ambiri omwe anaferedwa amakumana nazo.
-
ZIMENE ZINGAKUTHANDIZENI MUKAFEREDWA—ZIMENE MUNGACHITE PANOPA
Kodi mungatsatire njira ziti kuti musamavutike kwambiri ndi chisoni? Nkhaniyi ikufotokoza njira zingapo zomwe zathandizapo anthu ena. Njirazi zili ndi mfundo zochokera m’Baibulo.
-
MFUNDO ZOFUNIKA KWAMBIRI KWA ANTHU OMWE AFEREDWA
Werengani nkhaniyi kuti mudziwe njira zomwe ena atsatira pa nthawi yovutayi ndipo muone mmene inunso zingakuthandizireni.