Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mawu Oyamba

Mawu Oyamba

Ambiri timatha kudziwa ngati munthu wina ali ndi tsankho. Komatu n’zovuta kudziwa ngati ifeyo tili nalo.

Taonani mfundo zina zomwe zingatithandize kuthetsa tsankho.