Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Fufuzani Umboni

Fufuzani Umboni

Magazini ya Galamukani! ino ikufotokoza maumboni ena amene amasonyeza kuti zinthu zam’chilengedwechi zinachita kulengedwa. Fufuzani umboni umenewu ndipo onani ngati pali zifukwa zomveka zimene zingakuchititseni kukhulupirira kuti kuli Mlengi. M’munsimu, muli mitu ya mavidiyo komanso mabuku ena amene angakuthandizeni kupeza mfundo zina zothandiza. Mungapeze mitu imeneyi pa jw.org.

N’chifukwa chiyani anthu ambiri ophunzira amakhulupirira kuti kuli Mlengi?

Onerani zimene ena anafotokoza pa mavidiyo akuti Zokhudza Mmene Moyo Unayambira.”

Kodi pali mfundo zomveka zotsimikizira kuti zamoyo zinachita kusintha?

Werengani kabuku kakuti Kodi Zamoyo Zinachita Kulengedwa?

Kodi n’zomveka kukhulupirira kuti kuli Mlengi?

Onerani vidiyo yakuti Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Kukhulupirira Kuti Kuli Mulungu.

Kodi ndi nzeru kukhulupirira Baibulo?

Werengani kabuku kakuti Mmene Moyo Unayambira—Mafunso 5 Ofunika Kwambiri.