Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw.Org

Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw.Org

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Eliya​—Anapirira Mpaka Pamapeto

Eliya anakhalabe wokhulupirika ndipo anakwanitsa kupirira. Chitsanzo chake chingatithandize kulimbitsa chikhulupiriro chathu tikakumana ndi mavuto.

(Pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUKHULUPIRIRA MULUNGU.)

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Sindinkachedwa Kupsa Mtima

Munthu yemwe anali chigawenga amakhulupirira kuti mmene moyo wake ulili panopa ndi umboni wakuti Baibulo lili ndi mphamvu zotha kusintha munthu. Panopa ali pa ubwenzi wolimba ndi Mulungu.

(Pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDERE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)