NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) October 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira December 9, 2024–​January 5, 2025.

1924​—⁠Zaka 100 Zapitazo

M’chaka cha 1924, Ophunzira Baibulo anafunika kulimba mtima kuti apitirize kulalikira uthenga wabwino.

NKHANI YOPHUNZIRA 40

Yehova “Amachiritsa Anthu Osweka Mtima”

Idzaphunziridwa mlungu woyambira December 9-15, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 41

Zimene Tikuphunzira kwa Yesu pa Masiku Ake 40 Omaliza

Idzaphunziridwa mlungu wa December 16-22, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 42

Muziyamikira Amuna Amene Yehova Watipatsa Mumpingo

Idzaphunziridwa mlungu wa December 23-29, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 43

Kodi Tingatani Kuti Tisiye Kukayikira?

Idzaphunziridwa mlungu wa December 30, 2024–​January 5, 2025.

Kodi Mukudziwa?

Kodi nyimbo zinali zofunika bwanji m’nthawi ya Aisiraeli?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi khonde la kachisi wa Solomo linali lalitali bwanji?

Muzibwereza Mfundo Zikuluzikulu

Kodi nthawi zina mumavutika kukumbukira zimene mwaphunzira? Kodi n’chiyani chingakuthandizeni?