NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) December 2017

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa January 29 mpaka February 25, 2018.

“Ndikudziwa Kuti Adzauka”

N’chiyani chimatitsimikizira kuti akufa adzauka?

“Ndili ndi Chiyembekezo mwa Mulungu”

N’chifukwa chiyani tinganene kuti nkhani ya kuuka kwa akufa ili m’gulu la mfundo zazikulu zimene Akhristu amakhulupirira?

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwawerenga magazini aposachedwapa a Nsanja ya Olonda? Tayesani kuyankha mafunso.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi mwana woyamba kubadwa wa Aisiraeli ndi amene ankakhala mumzere wa makolo a Mesiya?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi kugwiritsa ntchito lupu (IUD) ngati njira ya kulera n’kogwirizana ndi Malemba?

Makolo, Thandizani Ana Anu Kupeza Nzeru Kuti Adzapulumuke

Makolo ambiri achikhristu amada nkhawa mwana wawo akakhala kuti akufuna kudzipereka kwa Mulungu ndi kubatizidwa. Kodi angathandize bwanji ana awo kuti adzapeze moyo wosatha?

Achinyamata, “Pitirizani Kukonza Chipulumutso Chanu”

Munthu akabatizidwa amakhala ndi udindo waukulu, koma achinyamata sayenera kuopa kapena kuzengereza kuti abatizidwe.

MBIRI YA MOYO WANGA

Ndinasiya Zinthu Zambiri Kuti Nditsatire Ambuye

Felix Fajardo anali ndi zaka 16 zokha pamene anasankha kukhala Mkhristu. Iye wakhala akutsatira Ambuye kulikonse kumene amutsogolera kwa zaka zoposa 70 ndipo sakunong’oneza bondo ngakhale pang’ono.

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2017

Mlozera nkhaniyu angakuthandizeni kupeza nkhani zosiyanasiyana zimene zinatuluka m’magazini a Nsanja ya Olonda m’chaka cha 2017.