Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2019
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA
BAIBULO
Akwanitsa Kuwerenga Mpukutu Wakale, June
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
N’chifukwa chiyani mtsikana wogwiriridwa “kuthengo” sankaimbidwa mlandu ngakhale kuti panalibe mboni ziwiri? (De 22:25-27), Dec.
MBIRI YA MOYO WANGA
Makolo Anga Anandithandiza Kuti Ndizitumikira Yehova (W. Mills), Feb.
Tinapeza ‘Ngale Yamtengo Wapatali’ (W. ndi P. Payne), Apr.
Yehova Wandidalitsa Kuposa Mmene Ndinkaganizira (M. Tonak), July
MBONI ZA YEHOVA
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
Chikhulupiriro Chimatipatsa Mphamvu, Aug.
Chitsanzo Chabwino pa Nkhani Yokhalabe Wosangalala (Yohane M’batizi), Aug.
“Muziyamika pa Chilichonse,” Dec.
Ubwino—Kodi Tingatani Kuti Tikhale ndi Khalidweli? Mar.
NKHANI ZOPHUNZIRA
Aisiraeli Ankafunika Kusonyeza Chikondi ndi Chilungamo, Feb.
“Anthu Okumvera” Adzapulumuka, Aug.
“Bwerani kwa Ine . . . Ndipo Ndidzakutsitsimutsani,” Sept.
Chikondi Chanu Chipitirire Kukula, Aug.
Chikundiletsa Kubatizidwa N’chiyani? Mar.
Kodi Mukukwaniritsa Mbali Zonse za Utumiki Wanu? Apr.
Kodi Mukusamalira ‘Chishango Chanu Chachikulu Chachikhulupiriro’? Nov.
Kodi Mumamudziwa Bwino Yehova? Dec.
Kodi Mzimu Woyera Umatithandiza Bwanji? Nov.
Kodi Tingateteze Bwanji Mtima Wathu? Jan.
Kodi Tingathandize Bwanji Anthu Amene Sakonda Zachipembedzo? July
Kodi Yehova Adzakuthandizani Kuchita Chiyani? Oct.
Lolani Kuti Yehova Akuthandizeni Polimbana ndi Mizimu Yoipa, Apr.
Makhalidwe Amene Amatichititsa Kupezeka Pamisonkhano, Jan.
Makolo Ayenera Kuphunzitsa Ana Awo Kukonda Yehova, Dec.
“Malizitsani” Zimene Munayamba Kuchita, Nov.
Muziyesetsa Kuti Kuphunzira Kuzikuthandizani, May
Mwambo wa Chikumbutso Umasonyeza Makhalidwe a Mfumu Yakumwamba, Jan.
“Ndinaona Khamu Lalikulu la Anthu,” Sept.
Pali Nthawi Yogwira Ntchito ndi Nthawi Yopuma, Dec.
Pezani Anzanu Apamtima Mapeto Asanafike, Nov.
‘Pitani Mukaphunzitse Anthu Kuti Akhale Ophunzira Anga,’ July
Pitirizani Kukhala ndi Mtima Wosagawanika, Feb.
‘Samalani Kuti Wina Angakugwireni,’ June
“Sitikubwerera M’mbuyo,” Aug.
Tidzakhalebe Okhulupirika pa “Chisautso Chachikulu,” Oct.
Tisapusitsidwe ndi “Nzeru za M’dzikoli,” May
Tizichita Zinthu Moganizira Ena, Mar.
Tizichotsa Maganizo Alionse Otsutsana ndi Kudziwa Mulungu, June
Tizidalira Yehova Tikakhala ndi Nkhawa, June
Tizigonjera Yehova ndi Mtima Wonse, Sept.
Tizikhala Odzipereka kwa Yehova Yekha, Oct.
Tizikonzekera Kuti Tidzathe Kupirira Pozunzidwa, July
Tizilambirabe Yehova Ngakhale Boma Litatiletsa, July
Tizilimbikitsa Anthu Amene Achitiridwa Zoipa, May
Tizimvetsera Mawu a Yehova, Mar.
Tizisonyeza Anthu Chifundo Tikakhala mu Utumiki, Mar.
Tizisonyeza Chikondi ndi Chilungamo M’dziko Loipali, May
Tizisonyeza Chikondi ndi Chilungamo Mumpingo, May
Tizisonyeza Kuti Ndife Oyamikira, Feb.
Tizitamanda Yehova Mumpingo, Jan.
Tizithandiza Anthu Amene Ali ndi Nkhawa, June
Tizitsanzira Yesu Kuti Tizikhala ndi Mtendere Wamumtima, Apr.
Tizitsatira Mfundo za Choonadi Pakachitika Maliro, Apr.
Tizitumikira Yehova Mwakhama Kumapeto kwa ‘Masiku Otsirizawa,’ Oct.
“Usayang’ane Uku ndi Uku Mwamantha, Pakuti Ine Ndine Mulungu Wako,” Jan.
Uthenga Wokhudza Aramagedo Ndi Wosangalatsa, Sept.
Yehova Amaona Kuti Atumiki Ake Odzichepetsa Ndi Amtengo Wapatali, Sept.
Yehova Anakonza Zoti Tikhale ndi Ufulu, Dec.
Yesetsani Kukhala Ofatsa Kuti Muzisangalatsa Yehova, Feb.
Zimene Tingachite Kuti Tizisangalalabe Utumiki Wathu Ukasintha, Aug.
Zimene Tingaphunzire M’buku la Levitiko, Nov.
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Kodi Ankayenda Bwanji Panyanja? Apr.
Kodi Masunagoge Anayamba Bwanji? Feb.
Msampha Wina wa Satana (zolaula), June
Mtumiki Woyang’anira Nyumba, Nov.
YEHOVA
YESU KHRISTU
Kodi N’zoona Kuti Anandifera Ineyo? July
NSANJA YA OLONDA YOGAWIRA