Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2023

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2023

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2023

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

KODI MUKUDZIWA?

Kodi zomwe ofukula zinthu zakale apeza ku Babulo, zokhudza njerwa zimasonyeza bwanji kuti Baibulo ndi lolondola? July

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

Kodi Aisiraeli ankapeza zakudya zina m’chipululu kupatula pa mana ndi zinziri? Oct.

Kodi zimene timakhulupirira pa nkhani yokhudza dzina la Yehova ndi ulamuliro wake zinamveketsedwa bwanji? Aug.

N’chifukwa chiyani “Uje” ananena kuti kukwatira Rute ‘kungawononge’ cholowa chake? (Rute 4:​1, 6), Mar.

Yesu atabadwa, n’chifukwa chiyani Yosefe ndi Mariya anakhalabe ku Betelehemu? June

MBIRI YA MOYO WANGA

Kuchita Chidwi ndi Ena Kumabweretsa Madalitso Osatha (R. Reid), July

Ndaona Anthu Okhulupirika Zinthu Zikuwayendera Bwino (R. Landis), Feb.

Ndimakhala Wosatekeseka Chifukwa Chodalira Yehova (I. Itajobi), Nov.

Zosangalatsa Zimene Ndapeza Komanso Zomwe Ndaphunzira Potumikira Yehova (R. Kesk), June

MBONI ZA YEHOVA

1923—Zimene Zinachitika Zaka 100 Zapitazo, Oct.

Hulda Anakwaniritsa Cholinga Chake, Nov.

Kuchitira Chifundo Anthu Onse, Dec.

MFUNDO ZOTHANDIZA POPHUNZIRA

Kodi mumakonda kuwerenga mbiri ya moyo wa abale ndi alongo athu? Jan.

Kodi mumapindula ndi malifalensi ofotokoza mavesi a m’Baibulo, opezeka mu Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani? Apr.

Kupeza Nkhani Zimene Zimaikidwa Patsamba Loyamba (jw.org), Feb.

Malifalensi a pa LAIBULALE YA PA INTANETI, May

Mmene Mungagwiritsire Ntchito Gawo Lakuti “Zatsopano” (JW Library® ndi jw.org), Mar.

Mmene Tingapezere Zinthu Zimene Zasintha Kamvedwe (Watch Tower Publications Index kapena Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani), Oct.

Muzifufuza Zambiri Zokhudza Makhalidwe a Yehova (Watch Tower Publications Index kapena Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani), Aug.

Muziloweza “Nyimbo Zauzimu” (jw.org), Nov.

Muziyamba ndi Zinthu Zofunika, July

Nkhani Zina Zopezeka mu Nsanja ya Olonda Yophunzira (JW Library®), June

Zoti Ana Achite (jw.org), Sept.

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

Anaona Chikondi cha Abale ndi Alongo, Feb.

Kodi Mumayendera Maganizo a Yehova pa Nkhani ya Mowa? Dec.

Ngati Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Amaonera Zolaula, Aug.

NKHANI ZOPHUNZIRA

Achinyamata, Kodi Mudzachita Chiyani pa Moyo Wanu? Sept.

Akhristu Achinyamata, Kodi Mungatani Kuti Mukhale Olimba Mwauzimu? Dec.

Akhristu Achitsikana, Kodi Mungatani Kuti Mukhale Olimba Mwauzimu? Dec.

Chikhulupiriro Komanso Ntchito Zake Zingachititse Kuti Tikhale Olungama, Dec.

“Chikondi Chimene Khristu Ali Nacho Chimatikakamiza,” Jan.

“Khalani Olimba, Osasunthika,” July

“Khalanibe Oganiza Bwino Ndipo Khalani Maso,” Feb.

Kodi Mwakonzekera Chisautso Chachikulu? July

Kodi Ndinu ‘Okonzeka Kumvera’? Oct.

Kodi Tingaphunzire Chiyani pa Zozizwitsa za Yesu? Apr.

Kodi Tingatani Kuti Tizikhulupirira Kwambiri Lonjezo la Yehova la Dziko Latsopano? Apr.

Kodi Tingatani Kuti Tizikondana Kwambiri? Nov.

Kodi Yehova Amayankha Mapemphero Anga? Nov.

Kufatsa Sikutanthauza Kufooka, Sept.

Kuopa Mulungu Kungatithandize Kuti Tipitirize Kulandira Madalitso, June

“Mlongo Wako Adzauka,” Apr.

Mmene Mungakonzekerere Kubatizidwa, Mar.

Mmene Yehova Amayankhira Mapemphero Athu, May

Mmene Yehova Anatsimikizira Lonjezo Lake la Paradaiso, Nov.

Mukhoza Kukhalabe Olimba Mtima pa Nthawi Yovuta, Nov.

Mungathe Kukwaniritsa Zolinga Zanu Zauzimu, May

Musamakayikire Kuti ‘Mawu a Mulungu Ndi Choonadi,’ Jan.

Musazimitse “Lawi la Ya,” May

Muzichita Khama Kuti Muzimvetsa Bwino Mawu a Mulungu, Oct.

Muzigwiritsa Ntchito Chilengedwe Pophunzitsa Ana Anu Zokhudza Yehova, Mar.

Muziphunzira Maulosi a M’Baibulo, Aug.

Muziphunzira pa Chitsanzo cha Danieli, Aug.

Muziphunzira Zambiri Zokhudza Yehova Poona Chilengedwe Chake, Mar.

Muzitsanzira Yehova pa Nkhani Yololera, July

Muziyamikira Mwayi Wanu Wolambira M’kachisi Wauzimu wa Yehova, Oct.

“Mwakutero, Onse Adzadziwa Kuti Ndinu Ophunzira Anga,” Mar.

N’chifukwa Chiyani Muyenera Kubatizidwa? Mar.

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuopa Yehova? June

Nyamulani Zinthu Zofunika Ndipo Tayani Zina Zonse, Aug.

Pitirizani Kukhala Oleza Mtima, Aug.

Pitirizani Kukonda Yehova ndi Anthu, July

Pitirizani Kukonzekera Tsiku la Yehova, June

Pitirizani Kuyenda pa “Msewu wa Chiyero,” May

“Sandulikani mwa Kusintha Maganizo Anu,” Jan.

Tili ndi Chiyembekezo Chomwe Sichitikhumudwitsa, Dec.

Tingakhalebe Okhulupirika Ngati Petulo, Sept.

Tizidalira Yehova Ngati Mmene Samisoni Ankachitira, Sept.

Tizilimbikitsana Pamisonkhano ya Mpingo, Apr.

Tiziyamikira Mphatso ya Moyo Imene Mulungu Anatipatsa, Feb.

Yehova “Adzakulimbitsani” Oct.

Yehova Adzakuthandizani Kupirira Mavuto Osayembekezereka, Apr.

Yehova Amadalitsa Khama Lathu Loyesetsa Kuti Tipezeke pa Chikumbutso, Jan.

Yehova Amatithandiza Kuti Zinthu Zizitiyendera Bwino, Jan.

Zimene Akulu Angaphunzire pa Chitsanzo cha Gidiyoni, June

Zimene Baibulo Limatiuza Zokhudza Mlembi Wake, Feb.

Zimene Tikuphunzira M’makalata Awiri a Petulo, Sept.

Zimene Tingachite Kuti Mapemphero Athu Azikhala Abwino Kwambiri, May

Zimene Tingachite Kuti Tizipindula Kwambiri Tikamawerenga Baibulo, Feb.

NSANJA YA OLONDA YOGAWIRA

Matenda a Maganizo—Mmene Baibulo Lingakuthandizireni, Na. 1

GALAMUKANI!

Kodi Dzikoli Lidzakhalanso Bwino? Pali Chiyembekezo, Na. 1