NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) December 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira February 3–March 2, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 48

Yesu Anapereka Chakudya Modabwitsa

Idzaphunziridwa mlungu woyambira February 3-9, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 49

Kodi Tiyenera Kuchita Chiyani Kuti Tidzapeze Moyo Wosatha?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira February 10-16, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 50

Muzithandiza Ana Anu Kulimbitsa Chikhulupiriro Chawo

Idzaphunziridwa mlungu woyambira February 17-23, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 51

Yehova Amakumbukira Misozi Yathu Yonse

Idzaphunziridwa mlungu woyambira February 24–March 2, 2025.

MBIRI YA MOYO WANGA

Ndakhala Ndikuphunzirabe Mpaka Pano

Joel Adams akufotokoza zimene zamuthandiza kuti azitumikira Yehova mosangalala kwa zaka zoposa 80.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi “angelo ochita kusankhidwa” otchulidwa pa 1 Timoteyo 5:21 ndi ndani?

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwawerenga mosamala magazini a chaka chino a Nsanja ya Olonda? Yesani kuona ngati mukukumbukira.

Anthu Okhulupirika kwa Yehova Amakwaniritsa Zimene Alonjeza

Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhani ya Yefita ndi mwana wake wamkazi?