NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) February 2025
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira April 14–May 4, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 6
Timayamikira Yehova Chifukwa Amatikhululukira
Idzaphunziridwa mlungu woyambira April 14-20, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 7
Timapindula ndi Kukhululuka kwa Yehova
Idzaphunziridwa mlungu woyambira April 21-27, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 8
Kodi Tingatsanzire Bwanji Kukhululuka kwa Yehova?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira April 28–May 4, 2025.
MBIRI YA MOYO WANGA
“Sindinakhalepo Ndekhandekha”
Onani chifukwa chake Angelito Balboa amakhulupirira kuti nthawi zonse Yehova ankakhala naye, ngakhale pamene akukumana ndi mayesero ovuta.
Muzipewa Mzimu Wodzikonda
Anthu ambiri m’dzikoli amaona kuti ndi ofunika kupatsidwa ulemu wapadera, ufulu komanso kuchitiridwa zinthu m’njira yapadera. Onani mfundo za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni kupewa maganizo amenewa.
Zimene Tingachite Kuti Tikhale Bwenzi Lenileni
Baibulo limanena kuti anzathu enieni amatithandiza pakagwa mavuto.
Funso Losavuta Limene Aliyense Angathe Kufunsa
Mofanana ndi Mary, mungathe kuyambitsa maphunziro a Baibulo angapo pongofunsa funso losavuta.
Kukhala Olimba Mtima Ena Akamatitsutsa
Kodi tingaphunzire chiyani pa kulimba mtima kwa Yeremiya ndi Ebedi-meleki?