NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) January 2025

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira March 3–April 6, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 1

M’patseni Yehova Ulemerero

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 3-9, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 2

Amuna, Muzilemekeza Akazi Anu

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 10-16, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 3

Muzisankha Zinthu Zimene Zingasangalatse Yehova

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 17-23, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 4

Kodi Dipo Limatiphunzitsa Chiyani?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 24-30, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 5

Madalitso Amene Timapeza Chifukwa cha Chikondi cha Yehova

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 31–April 6, 2025.

Kujambula Kumathandiza Kuti Tizikumbukira Zinthu

Mutha kumakumbukira zimene mumawerenga ngati mumaziona m’maganizo mwanu.