Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw.Org

Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw.Org

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Kaulukidwe Kodabwitsa ka Ntchentche

Ntchentche zamtundu winawake zimatha kutembenuka mofanana ndi ndege zankhondo ndipo zimachita zimenezi sekondi imodzi isanathe. Kodi zinangochitika zokha kuti ntchentchezi zikhale ndi luso limeneli?

(Pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI.)

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Zinkaoneka Ngati Zinthu Zikundiyendera

Stéphane anali wachinyamata, wotchuka, ndipo ankapanga ndalama zambiri koma akakhala kwayekha sankapeza mtendere mumtima. Kodi zinatani kuti zinthu ziyambe kuyendadi bwino pa moyo wake?

(Pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDERE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)