NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) November 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira January 6–​February 2, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 44

Zimene Tingachite Ena Akatilakwira

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 6-12, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 45

Zimene Tikuphunzira pa Mawu Omaliza a Amuna Okhulupirika

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 13-19, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 46

Kodi Mukuyesetsa Kuti Mukhale Mtumiki Wothandiza?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 20-26, 2025.

NKHANI YOPHUNZIRA 47

Kodi Mukuyesetsa Kuti Mukhale Mkulu?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 27–February 2, 2025.

MBIRI YA MOYO WANGA

Yehova Ankatilimbikitsa pa Nthawi Yankhondo Komanso Yamtendere

Paul ndi Anne Crudass akufotokoza mmene Yehova wakhala akuwalimbikitsira pa nthawi ya nkhondo komanso pamene ankakumana ndi mayesero aakulu.

Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muziphunzira Mlungu Uliwonse

Onani mfundo 4 zimene zingakuthandizeni kuti muziphunzira mlungu uliwonse ndipo muzisangalala pophunzira.

Muzipeza Malo Abwino Ophunzirira

Onani mfundo zitatu zomwe zingakuthandizeni kuti muzipindula kwambiri mukamaphunzira.