NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) September 2018

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa October 29 mpaka December 2, 2018

“Ngati Zimenezi Mukuzidziwa, Ndinu Odala Mukamazichita”

Kodi tingatani kuti tikhalebe odzichepetsa, nanga n’chifukwa chiyani tiyenera kuchita zimenezi?

Akhristu Achikulire, Yehova Amayamikira Kukhulupirika Kwanu

Kodi akulu achikulire a masiku ano asonyeza bwanji kudzichepetsa?

Pitirizani Kusonyeza Chikondi Chifukwa Chimalimbikitsa

Onani zimene tingachite kuti tizilimbikitsana m’masiku ovuta ano.

Anthu Amene Amatumikira “Mulungu Wachimwemwe” Amakhala Osangalala

Kodi tingatani kuti tizikhalabe achimwemwe ngakhale kuti timakumana ndi mavuto?

Nthawi Ili Bwanji?

Kodi anthu otchulidwa m’Baibulo ankatchula bwanji nthawi?

Yehova Ndi Wamphamvuyonse Koma Amaganizira Ena

Kodi Yehova amapereka bwanji chitsanzo chabwino pa nkhani yochita zinthu moganizira ena?

Tizikhala Okoma Mtima Komanso Oganizira Ena Ngati Yehova

Phunzirani njira zimene tingasonyezere kuti timaganizira ena m’banja, mumpingo komanso mu utumiki.