Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2022

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2022

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

KODI MUKUDZIWA?

  • Kodi Aroma ankalola kuti munthu amene waphedwa popachikidwa pamtengo aikidwe m’manda ngati anthu ena onse? June

  • Kodi kale anthu ankadziwa bwanji pamene payambira mwezi kapena chaka? June

  • Kodi n’zoona kuti kunali munthu wotchedwa Moredekai? Nov.

  • N’chifukwa chiyani Aisiraeli ankapereka malowolo? Feb.

  • N’chifukwa chiyani zinali zothandiza kuti munthu azitha kupereka njiwa kapena nkhunda? Feb.

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

  • Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani ya malumbiro? Apr.

  • Kodi Davide ankanena zosatheka pomwe analemba kuti adzatamanda Mulungu “mpaka muyaya”? (Sl 61:8), Dec.

  • Kodi mtumwi Paulo ankatanthauza chiyani pomwe anadzitchula kuti anali ngati “khanda lobadwa masiku asanakwane”? (1Ak 15:8), Sept.

  • Kodi ndi anthu ati omwe adzaukitsidwire padzikoli, nanga kuuka kwake kudzakhala kotani? Sept.

  • Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti: “Musaganize kuti ndinabweretsa mtendere”? (Mt 10:34, 35), July

  • Kodi zinachitika m’njira yotani kuti Davide ‘amvere chisoni Mefiboseti’ koma kenako n’kumupereka kuti aphedwe? (2Sa 21:7-9), Mar.

  • Mmene tiyenera kuonera ukwati wakale ndi watsopano Mkhristu akathetsa banja, Apr.

MBIRI YA MOYO WANGA

  • Ndakhala Ndikusangalala Kuphunzira Komanso Kuphunzitsa Zokhudza Yehova (L. Weaver, Jr.), Sept.

  • Ndinalola Kuti Yehova Azinditsogolera pa Moyo Wanga (K. Eaton), July

  • Ndinapeza Chinthu Choposa Ntchito ya Udokotala (R. Ruhlmann), Feb.

  • “Ndinkafuna Kutumikira Yehova” (D. van Marl), Nov.

MBONI ZA YEHOVA

  • 1922​—Zimene Zinachitika Zaka 100 Zapitazo, Oct.

MOYO NDI MAKHALIDWE A CHIKHRISTU

  • Anapatsa Agalu Anga Mabisiketi (ulaliki wapashelefu), Apr.

  • Kodi Ndinu Wokonzeka ‘Kudzalandira Dziko Lapansi’? Dec.

  • “Lamulo la Kukoma Mtima Kosatha” Lizikutsogolerani, June

  • N’chifukwa Chiyani Masiku Ano Sitimenya Nkhondo Ngati Mmene Ankachitira Aisiraeli? Oct.

  • Zimene Zingatithandize Tikakhala ndi Nkhawa, Apr.

NKHANI ZOPHUNZIRA

  • Achinyamata, Pitirizani Kupita Patsogolo Mwauzimu Pambuyo Pobatizidwa, Aug.

  • Akulu, Pitirizani Kutsanzira Mtumwi Paulo, Mar.

  • Anthu a Yehova Amakonda Chilungamo, Aug.

  • Chifukwa Chake Timapezeka pa Chikumbutso, Jan.

  • ‘Imva Mawu a Anthu Anzeru,’ Feb.

  • “Iwe Udzakhala Ndi Ine M’Paradaiso,” Dec.

  • Kodi Chikondi Chingatithandize Bwanji Kuti Tisamachite Mantha, June

  • Kodi Dzina Lanu Lili “M’buku la Moyo”? Sept.

  • Kodi Malangizo Amene Mumapereka ‘Amasangalatsa Mtima’? Feb.

  • Kodi Mukuona Zimene Zekariya Anaona? Mar.

  • Kodi Mumakhulupirira Kuti Yehova Amachita Zinthu M’njira Yoyenera? Feb.

  • Kodi Ndinu “Chitsanzo . . . M’kalankhulidwe”? Apr.

  • Kulambira Koona Kumachititsa Kuti Muzisangalala Kwambiri, Mar.

  • ‘Kuthandiza Anthu Ambiri Kuti Akhale Olungama,’ Sept.

  • Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikonda Yehova, May

  • Mmene Yehova Amatithandizira Kukwaniritsa Utumiki Wathu, Nov.

  • Mmene Yehova Amatithandizira Kuti Tizipirira Mosangalala, Nov.

  • Mukhoza ‘Kuvula Umunthu Wakale,’ Mar.

  • Mungapeze Chimwemwe Chenicheni, Oct.

  • Mungathe Kupeza Mtendere pa Nthawi ya Mavuto, Dec.

  • Musalole Kuti Chilichonse Chikusiyanitseni ndi Yehova, Nov.

  • “Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi Yanu,” Jan.

  • Muzikhalabe Oganiza Bwino Mukamayesedwa, Nov.

  • Muzikhulupirira Abale Anu, Sept.

  • Muzisangalala ndi Zonse Zomwe Mukuchita Potumikira Yehova, Apr.

  • Muzisonyeza Kuti Ndinu Wodalirika, Sept.

  • Muzithandiza Ena Kupirira pa Nthawi Zovuta, Dec.

  • Muzitsanzira Yesu Potumikira Ena, Feb.

  • Muziyamikira Mwayi Wanu wa Pemphero, July

  • Nzeru Yeniyeni Ikufuula, Oct.

  • Nzeru Zothandiza pa Moyo Wathu, May

  • Odala Ndi Anthu Okhulupirika Kwa Yehova, Oct.

  • “Ofunafuna Yehova Sadzasowa Chilichonse Chabwino,” Jan.

  • Pitirizani “Kulimbikitsana,” Aug.

  • Pitirizani Kulimbitsa Chiyembekezo Chanu, Oct.

  • ‘Pitirizani Kuyenda M’choonadi,’ Aug.

  • Pitirizani Kuvala “Umunthu Watsopano” Pambuyo Pobatizidwa, Mar.

  • Tingakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, Dec.

  • Tingatani Kuti Tizikhala ndi Zolinga Zauzimu N’kumazikwaniritsa? Apr.

  • Tizithandiza Mtsogoleri Wathu Yesu, July

  • Ufumu Ukulamulira, July

  • Ulosi Wakalekale Umene Umakukhudzani, July

  • Yehova Amadalitsa Anthu Omwe Amakhululuka, June

  • Yehova Amakhululuka Kwambiri Kuposa Aliyense, June

  • Yehova Amayang’anira Anthu Ake, Aug.

  • “Yembekezera Yehova,” June

  • Zimene Azimayi Angaphunzire kwa Yunike, Apr.

  • Zimene Tikuphunzira pa Misozi ya Yesu, Jan.

  • Zimene Tingaphunzire Kuchokera kwa Mng’ono Wake wa Yesu, Jan.

  • Zimene Zili M’buku la Chivumbulutso Zimakhudzanso Adani a Mulungu, May

  • Zimene Zili M’buku la Chivumbulutso Zimakhudza Tsogolo Lanu, May

  • Zimene Zili M’buku la Chivumbulutso Zimakukhudzani, May

NSANJA YA OLONDA YOGAWIRA

  • Kodi N’zotheka Kuthetsa Chidani? Na. 1

GALAMUKANI!

  • Kodi Mungatani Kuti Mupirire Mavuto a M’Dzikoli? Na. 1