NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) April 2019

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa June 3-30, 2019.

Kodi Mukukwaniritsa Mbali Zonse za Utumiki Wanu?

Kodi tingatani kuti tizilalikira mogwira mtima komanso tizisangalala mu utumiki?

Tizitsanzira Yesu Kuti Tizikhala ndi Mtendere Wamumtima

Pali zinthu zitatu zimene Yesu ankachita zomwe zingatithandize kuti tizikhala ndi mtendere wamumtima, ngakhale pamene tikukumana ndi mavuto.

Tizitsatira Mfundo za Choonadi Pakachitika Maliro

Kodi tingapewe bwanji kuchita nawo miyambo yosemphana ndi Malemba pakachitika maliro?

Lolani Kuti Yehova Akuthandizeni Polimbana ndi Mizimu Yoipa

Kodi tingatani kuti tisasocheretsedwe ndi Satana komanso ziwanda zake?

MBIRI YA MOYO WANGA

Tinapeza ‘Ngale Yamtengo Wapatali’

Werengani nkhani ya moyo wosangalala wa a Winston ndi a Pamela Payne a ku Australia.

Kodi Mukudziwa?

Kodi anthu akale ankayenda bwanji panyanja?