NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) December 2021

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira January 31–February 27, 2022.

NKHANI YOPHUNZIRA 48

“Mukhale Oyera”

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwasangalala kuwerenga magazini a posachedwapa a Nsanja ya Olonda? Yesani kuona ngati mukukumbukira.

NKHANI YOPHUNZIRA 50

Muzimvera M’busa Wabwino

NKHANI YOPHUNZIRA 51

Pitirizani ‘Kumumvera’

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2021

Mlozera nkhani wa nkhani zonse zotuluka m’magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2021, ndipo zalembedwa motsatira mitu yake.