Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000
Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
Buku Labwino? 12/1
Chaka Chabwino Kwambiri Kugaŵira, 1/15
Mauthenga Abwino—Mbiri Kapena Nthano? 5/15
Mauthenga Obisika? 4/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Anadandaula Ndani za Mafuta Amene Yesu Anadzozedwa? 4/15
Angakane Kusudzulidwa, 12/15
Kodi Kunakomera Yehova Kutundudza Kristu? (Yes. 53:10), 8/15
Magazi Ako Omwe, 10/15
Mkwiyo wa Ndani? (Aroma 12:19), 3/15
Zotengedwa M’magazi? 6/15
MBONI ZA YEHOVA
Altiplano ku Peru, 11/15
Anafupidwa Atafufuza kwa Nthaŵi Yaitali (Denmark), 9/1
Buku la Danieli Lifotokozedwa! (Buku la Ulosi wa Danieli), 1/15
Chilumba cha Robinson Crusoe, 6/15
“Chitsanzo cha Mgwirizano,” 10/15
India, 5/15
Italy, 1/15
Kudera Lamapiri la Chiapas (Mexico), 12/15
Kulengeza Ufumu ku Fiji, 9/15
Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15
Kusodza Anthu ku Nyanja ya Aegean, 4/15
Mamembala Atsopano a Bungwe Lolamulira, 1/1
Matupi Aang’ono, Mitima Yabwino, 2/15
Misonkhano Yachigawo yakuti “Mawu Aulosi a Mulungu,” 1/15
Mtima Wamataya Umadzetsa Chimwemwe (zopereka), 11/1
Poponderezedwa ndi Anazi (Netherlands), 4/1
Senegal, 3/15
Taiwan, 7/15
Tuvalu, 12/15
Ulendo wa ku Zilumba za M’nyanja ya Pacific—Kuntchito! 8/15
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Abusa Achikristu, ‘Tsegulani Mtima Wanu’! 7/1
Kodi Anthu Achiwawa Mumawaona Monga Momwe Mulungu Amawaonera? 4/15
Kodi Kukhala Mkristu N’chiyani? 6/1
Kodi Kupambana Mumati N’kutani? 11/1
Kodi Mukupindula ndi Zitsanzo Zabwino? 7/1
Kodi Mumadziona Motani? 1/15
Kodi Mumatani Pakakhala Kusamvana? 8/15
Kodi N’chifukwa Chiyani Alibe Ana? 8/1
Kodi Ndinu Mkristu ‘Wokhwima Ndithu’? 8/15
Kodi Ndinu Wozindikira? 10/1
Kudzichepetsa—Mkhalidwe Umene Umalimbikitsa Mtendere, 3/15
Kufunafuna Yehova ndi Mtima Wokonzekera, 3/1
Kukhala Oganiza Bwino pa Zoyembekeza Zathu, 8/1
Kulemekeza Ulamuliro, 8/1
Kupanga Mzimu Woyera Kukhala Mthandizi Wanga, 10/15
Maukwati Osangalatsa Amene Amalemekeza Yehova, 5/1
Mmene Mungayandikirire kwa Mulungu, 10/15
Mukhoza Kudzisunga M’dziko Lachiwerewereli (Miy. 5), 7/15
Mukudzivomereza Nokha kwa Ena, 4/15
N’chifukwa Chiyani Mumatumikira Mulungu? 12/15
N’kukhaliranji Wodzimana? 9/15
Nyimbo Zomwe Zimakondweretsa Mulungu, 6/1
Pangani Ubwenzi Wathithithi ndi Yehova (Miy. 3), 1/15
Pezani Chitonthozo M’nyonga ya Yehova, 4/15
“Sunga Malangizo Anga, Nukhale ndi Moyo” (Miy. 7), 11/15
“Tchinjiriza Mtima Wako” (Miy. 4), 5/15
Tetezani Dzina Lanu, (Miy. 6), 9/15
Timafunikira Gulu Lolinganizidwa la Yehova, 1/1
Tumikirani Mulungu ndi Mzimu Wofunitsitsa, 11/15
Uphungu Wanzeru wa Mayi (Miy. 31), 2/1
MBIRI YA MOYO WANGA
Anandidalitsa ndi Choloŵa Chapadera (C. Allen), 10/1
Kukumbukira Mlengi Wathu Kuyambira Paunyamata (D. Hibshman), 1/1
Kusafuna Zambiri M’moyo Potumikira Yehova (C. Moyer), 3/1
Kusiya Ntchito Yopanga Zida Kuyamba Ntchito Yopulumutsa Miyoyo (I. Ismailidis), 8/1
Kuthokoza Yehova—Kupyolera mu Utumiki wa Nthaŵi Zonse! (S. Reynolds), 5/1
Ndinathandizidwa Kuthetsa Manyazi (R. Ulrich), 6/1
“N’takhala ndi Chikhulupiriro Chosafooka”! (H. Müller), 11/1
Nthaŵi Zonse Yehova Amafupa Anthu Ake Okhulupirika V. Duncombe), 9/1
“Simudziŵa Chimene Chidzagwa Maŵa” (H. Jennings), 12/1
Wonyamula Kuunika ku Mayiko Ambiri (G. Young), 7/1
Yehova Ndiye Pothaŵirapo Panga ndi Mphamvu Yanga (M. Filteau), 2/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
Akristu Amapeza Chimwemwe Potumikira, 11/15
Chirikizani Chiphunzitso Chaumulungu Molimbika, 5/1
Chiyembekezo cha Chiukiriro N’champhamvu, 7/15
Chiyembekezo cha Chiukiriro N’chotsimikizirika! 7/15
Choloŵa Chathu Chamtengo Wapatali—Kodi Chimatanthauzanji kwa Inu? 9/1
“Dikirani,” 1/15
Dziko Latsopano—Kodi Mudzakhalamo? 4/15
‘Dzipulumutseni Nokha Ndi Iwo Akumva Inu,’ 6/1
“Funani Yehova, ndi Mphamvu Yake,” 3/1
Imani Amphumphu ndi Otsimikiza Kotheratu, 12/15
Imvani Chimene Mzimu Unena, 5/1
“Inu Nonse Muli Abale,” 6/15
Khalanibe ndi “Chiyembekezo cha Chipulumutso” Choŵala! 6/1
Khalani ndi Chikhulupiriro M’mawu Aulosi a Mulungu! 5/15
Kodi Atumiki a Mulungu Ndani Lerolino? 11/15
Kodi Muli ndi “Mtima Wa Kristu”? 2/15
Kodi Mwasonkhezeredwa Kukhala Monga Yesu? 2/15
Kodi Oipa Adzakhalabe Kwa Utali Wotani? 2/1
Kodi Zikumbutso za Yehova Mumazikonda Kwambiri? 12/1
Kudzikuza Kumadzetsa Manyazi, 8/1
Kudziŵa “Mtima wa Kristu,” 2/15
Kufesa Mbewu za Choonadi cha Ufumu, 7/1
Kupanga Zinthu Zonse Kukhala Zatsopano—Monga Kunanenedwera, 4/15
Kupatula Nthaŵi Yoŵerenga ndi Kuphunzira, 10/1
Kuphunzira—N’kothandiza ndi Kokondweretsa, 10/1
Kusangalala Mwa Mulungu wa Chipulumutso Chathu, 2/1
Kutumikira Limodzi ndi Mlonda, 1/1
Kuŵerenga Baibulo—N’kopindulitsa ndi Kosangalatsa, 10/1
Labadirani Mawu Aulosi a Mulungu, 4/1
Labadirani Mawu Aulosi a Mulungu a M’tsiku Lathu, 5/15
Lalikani Uthenga Wabwino Mwachangu, 7/1
Lemekezani Anthu Opatsidwa Ulamuliro Pa Inu, 6/15
Lingaliro Laumulungu la Khalidwe Loyera, 11/1
Mmene Yehova Akutitsogolera, 3/15
‘Mulungu, Tumizani Kuunika Kwanu,’ 3/15
Mungakhalebe ndi Khalidwe Loyera, 11/1
Nsembe Zimene Zinakondweretsa Mulungu, 8/15
Nsembe Zotamanda Zimene Zimakondweretsa Yehova, 8/15
“Nthaŵi Yake Siinafike,” 9/15
“Nzeru Ili ndi Odzichepetsa,” 8/1
Omenyana Ndi Mulungu Sadzapambana, 4/1
Sonyezani Mtima wa Kristu, 9/1
Sonyezani Mtima Wodikira! 9/1
Thandizani Ena Kuyenda Moyenera Yehova, 12/15
Ufumu wa Mulungu—Ulamuliro Watsopano wa Dziko Lapansi, 10/15
“Wamng’ono” Wasanduka “Chikwi,” 1/1
“Yafika Nthaŵi”! 9/15
Yehova Amapereka Mphamvu kwa Wotopa, 12/1
Yehova—Iye Amene Ali Wolimba Mphamvu, 3/1
Yehova Sadzachedwa, 2/1
Zimene Ufumu wa Mulungu Udzachita, 10/15
“Zinthu Zofunika” Zikudzaza Nyumba ya Yehova, 1/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
“Abale a ku Poland,” 1/1
Antiokeya (Syria), 7/15
Chidani, Kodi chidzatha? 8/15
Chikhulupiriro Chingasinthe Moyo Wanu, 1/1
Chinsinsi cha Chipambano, 2/1
Cyril Lucaris—Mwamuna Yemwe Anaona Baibulo Kukhala Lofunika, 2/15
Dziko Lopanda Nkhaŵa, 9/15
Kodi Apezanji pa Yezreeli? 3/1
Kodi Malangizo Abwino Mungawapeze Kuti? 6/1
Kodi Muyenera Kufufuza za Zipembedzo Zina? 10/15
Kodi Muyenera Kuwakhulupirira? 12/1
Kodi Mzimu wa Mulungu Umagwira Ntchito Motani Lerolino? 4/1
Kugwira Ntchito “M’munda”—Nyengo Yotuta Isanafike, 10/15
Kukongola kwa M’kati, 11/15
Kupemphera Kumathandizadi? 11/15
Kuthetsa Ziphuphu, 5/1
‘Kuzungulira Guwa la Nsembe Lanu,’ 5/1
Makhalidwe a M’Baibulo Ndiwo Ali Abwino Koposa, 11/1
Malo Ongoyeserapo Anthu, 10/1
‘Mbuzi ya Kumapiri ya Maonekedwe Osiririka,’ 10/1
Mgwirizano pa Kupembedza Ukuoneka kuti Ungatheke? 12/1
Miyambo ya Khirisimasi—Kodi Ndi Yachikristu? 12/15
Mmene Mungapezere Mabwenzi, 12/1
Mmene Moyo Wanu Ungakhalire ndi Tanthauzo Lalikulu, 7/15
Moyo Wangwiro Si Loto Chabe! 6/15
Mtendere wa Dziko Lonse Udzakhalapo Motani? 11/1
Mtengo wa Azitona, 5/15
Mulungu Amayankha Mapemphero, 3/1
Mumadziŵa Kudikira? 9/1
Mumakhulupirira Zomwe Simungathe Kuziona? 6/15
Mungapeze Mtendere wa Mumtima, 7/1
Mverani Chenjezo! 2/15
Mwamuna Wachitsanzo Chabwino Amene Anavomera Kum’langiza, (Yobu) 3/15
N’kugonjetseranji Malingaliro Osafuna Kulakwitsa Kanthu? 6/15
“Nthaŵi za Kukonzanso” Zayandikira! 9/1
Osuliza, 7/15
Nyama za M’Baibulo, 2/15
Tingaphunzire ku Banja Loyamba la Anthu, 11/15
Ufiti?, 4/1
Wozunza Aona Kuunika Kwakukulu (Paulo), 1/15
Yosiya, 9/15
OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 8/1, 9/1, 12/1
YEHOVA
Kodi Yehova Adzakukumbukirani Motani? 2/1
Mulungu Amayankha Mapemphero, 3/1
Wamkulu Kuposa Mitima Yathu, 5/1
YESU KRISTU
Mmene Yesu Kristu Angatithandizire, 3/15