Kodi Mungafune Kukuchezerani?
Kodi Mungafune Kukuchezerani?
Ngakhale m’dziko lino lodzala ndi mavuto, mungapeze chimwemwe mwa kukhala ndi chidziŵitso cholongosoka cha Baibulo chonena za Mulungu, Ufumu wake, ndi chifuno chake chabwino kwambiri kwa anthu. Ngati mungafune kudziŵa zambiri kapena kuti wina adziphunzira nanu Baibulo panyumba panu kwaulere, lemberani ku Watchtower, Box 30749, Lilongwe 3, Malaŵi, kapena ku adiresi yoyenera pa maadiresi osonyezedwa patsamba 2.