Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2001

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2001

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2001

Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo

BAIBULO

Buku Lokhala ndi Mabuku Onse a M’Baibulo, 5/1

Cyril ndi Methodius​—Otembenuza, 3/1

Kuyamikira Baibulo la New World Translation, 11/15

Kumvetsa Baibulo, 7/1

Mipukutu ya ku Nyanja Yakufa, 2/15

N’kuphunziriranji Baibulo, 7/1

MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA

Kodi akristu oona ayenera kuchiona motani chizoloŵezi chofala chopatsana ulere mapulogalamu ogulitsa a pakompyuta? 2/15

Kodi Danieli anali kuti pamene Ahebri atatu aja anawayesa kuti alambire fano lagolide? (Da 3), 8/1

Kodi kudzoza “Malo Opatulikitsa” kunachitika liti? (Da 9:24), 5/15

Kodi kulambira Yehova “mumzimu” kumatanthauzanji? (Yoh 4:24), 9/15

Kodi njoka ija m’munda wa Edene inalankhula motani? 11/15

Kodi Tiyenera Kupempherera Munthu Wochotsedwa? (Yer 7:16),12/1

Kodi Yehova anapangana naye pangano Abrahamu ali ku Uri kapena ku Harana? 11/1

Kodi Yobu anavutika kwa nthaŵi yaitali motani? 8/15

Kulowa mpumulo wa Yehova (Aheb. 4:9-11), 10/1

“Kupembedza mafano kosaloleka,” (1Pe 4:3), 7/15

Mitengo yonyamulira likasa la chipangano (1Maf.8:8), 10/15

“Miyamba” (2Pe 3:13) ndi “kumwamba” (Chiv. 21:1), 6/15

Mkazi wachikristu ndi zochitika za maholide, 12/15

N’chifukwa chiyani kuli kofunika kwa Akristu kuulula machimo awo kwa akulu mu mpingo? 6/1

Zinthu zonse zinalengedwa “kwa” Yesu motani? (Akol 1:16), 9/1

MBIRI YA MOYO WANGA

Anapirira ‘Kufikira Chimaliziro’ (L. Swingle), 7/1

Kuchirikizidwa ndi Yehova (F. Lee), 3/1

Kukatumikira Kulikonse Kumene Ndinkafunika (J. Berry), 2/1

Kutsatabe Njira ya Yehova (L. Valentino), 5/1

Kutumikira ndi Moyo Wonse Mosasamala Kanthu za Mayesero (R. Lozano), 1/1

Kuunika Kwauzimu Kukuwala ku Middle East (N. Salem), 9/1

Kuvomera Yehova Akamatipempha (M. Zanardi), 12/1

Moyo Waulemerero Potumikira Yehova (R. Kurzen), 11/1

Ndimayamikira Chifukwa Chokumbukira Zinthu Zamtengo Wapatali! (D. Caine), 8/1

Tinamuyesa Yehova (P. Scribner), 7/1

Tinkachitira Zinthu Limodzi (M. Barry), 4/1

Wosangalala ndi Wothokoza Ngakhale pa Vuto Losautsa Mtima (N. Porter), 6/1

“Yehova Wandichitira Zabwino Zambiri!”(K. Klein), 5/1

Zochitika Zosayembekezeka (E. & H. Beveridge), 10/1

MBONI ZA YEHOVA

Analandira Satifiketi Chifukwa cha Kuchita Bwino (Congo [Kinshasa]), 8/15

Anapambana Chizunzo cha Nazi, 3/15

Apambana Mlandu M’khoti Lapamwamba la Federal Constitution (Germany), 8/15

Dokotala wa Maso Afesa Mbewu (Ukraine, Israel), 2/1

France, 8/15, 9/1

Kale Tinali Mimbulu​—Tsopano Ndife Nkhosa! 9/1

Kenya, 2/15

Kodi Ntchito Iyi Ingakhale Yabwino Kwambiri kwa Inu? (Utumiki wa pa Beteli), 3/15

Kumaliza Maphunziro a Gilead, 6/15, 12/15

Kusamalirana Muubale Wapadziko Lonse (Othawa Nkhondo), 4/15

Kuthandiza Achinyamata, 7/15

Madzi Opatsa Moyo ku Andes, 10/15

Misonkhano ya Chigawo ya “Akuchita Mawu a Mulungu,” 1/15

Misonkhano ya Chigawo ya “Aphunzitsi a Mawu a Mulungu,” 2/15

Misonkhano Yaikulu Ndi Umboni Wosangalatsa wa Ubale Wathu, 9/15

Mmene Bungwe Lolamulira Limasiyanirana ndi Bungwe Lalamulo, 1/15

Msonkhano Wapachaka wa 2000, 1/15

“Ntchito Yaukatswiri” (Seŵero la Pakanema), 1/15

Sitinali Tokha Pamene Chikhulupiriro Chathu Chinali Kuyesedwa (Magazi), 4/15

‘Thokozani Mboni za Yehova Chifukwa cha Ufulu Wachipembedzo,’ 5/15

“Tidzaonana mu Ufumu wa Mulungu” (F. Drozg), 11/15

Timachita Zonse Zomwe Tingathe! (Amishonale), 10/15

“Tsiku Lokambirana za Zipembedzo” (Sukulu za ku Poland), 11/1

MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU

Anthu Sakumvetsetsani? 4/1

Chikhulupiriro Chenicheni, 10/1

Gonjetsani Zinthu Zokulepheretsani Kupita Patsogolo, 8/1

Kodi Mulidi Ololera? 7/15

‘Kugwiritsa Ntchito Nthaŵi Moyenera,’ 5/1

Kukayika, 7/1

Kukulitsa Khalidwe Labwino, 1/15

Kulapa, 6/1

Kumvera​—Phunziro Lofunika Paubwana, 4/1

Kupeŵa Matenda a Mtima Wauzimu, 12/1

Kupitirizabe Polefulidwa! 2/1

Kusankha Mwanzeru, 9/1

Kuthandiza Akazi Amasiye, 5/1

Kwaniritsani Zomwe Ana Anu Amafunikira! 12/15

Limbikitsani Chikhulupiriro mwa Yehova, 6/1

‘Madalitso Ali pa Wolungama,’ 7/15

“Madalitso a Yehova Alemeretsa,” 11/1

“Motero Thamangani,” 1/1

Mumatani Pakachitika Chinyengo, 11/15

Mungachite Moyenera Ngakhale Sanakulereni Bwino, 4/15

‘Ndi Nzeru Masiku Athu Adzachuluka’ (Miy. 9), 5/15

Samalirani Ana ndi Akazi Amasiye, 6/15

Tetezani Chikumbumtima, 11/1

Udani​—Woyenera ndi Wosayenera, 2/15

‘Wodala Munthu Wopeza Nzeru’’ (Miy. 8), 3/15

Yendani ‘M’njira Yoongoka’ (miy. 10), 9/15

Zomwe Munazoloŵera Kuchita, 8/1

Zoyenera Kuchita Ngati Mukuvutika Maganizo, 4/15

NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA

Abrahamu Anali Chitsanzo cha Chikhulupiriro, 8/15

Anthu Obwezeretsedwa a Yehova Akum’tamanda Padziko Lonse Lapansi, 2/15

Chikristu Choona Chikupambana! 4/1

Chipulumutso Kwa Osankha Kuunika, 3/1

Chisangalalo Kwa Oyenda M’kuunika, 3/1

‘Funafunani Mtendere ndi Kuulondola,’ 9/1

Funafunani Yehova Lisanadze Tsiku La Mkwiyo Wake, 2/15

Ganizirani Ntchito Zodabwitsa za Mulungu, 4/15

Khalanibe Osasunthika Ngati Oona Wosaonekayo! 6/15

Khalani Ndi Chikhulupiriro Monga cha Abrahamu! 8/15

Khalani ndi Mtima woopa Yehova, 12/1

Khalani ndi Mtima Wovomerezeka kwa Yehova, 10/15

Kodi Chikondi Chanu N’chosefukira Motani? 1/1

Kodi Madalitso A Yehova Adzakupezani? 9/15

Kodi Mtendere wa Kristu Ungachite Motani Ufumu M’mitima Yathu? 9/1

Kodi Mukuchita Mogwirizana Ndi Kudzipatulira Kwanu? 2/1

Kodi Mutha “Kusiyanitsa Chabwino ndi Choipa”? 8/1

Kodi Mwana “Wosakaza” Mungamuthandize Bwanji? 10/1

Kodi Mwapanga Choonadi Kukhala Chanuchanu? 2/1

Kondwerani ndi Mulungu Wachimwemwe, 5/1

Kondwerani Nthaŵi Zonse Potumikira Yehova, 5/1

Kondwerani Pakuti Mwadziŵa Yehova, 7/1

Kugonjetsa Kufooka Kwaumunthu, 3/15

Kulani M’chikondi, 1/1

Kumanga Banja Lolimba Mwauzimu, 5/15

Kupita Patsogolo Kukagonjetsa Komaliza! 6/1

Limbikirani Ntchito Yotuta! 7/15

Madalitso A Yehova Amatilemeretsa, 9/15

Malangizo a Mulungu Othandiza Posankha Wokwatirana Naye, 5/15

Mankhwala Omwe Angathandize Kuthetsa Nkhaŵa, 12/15

‘Mawu a Yehova Anapitirizabe Kukula,’ 4/1

Musakhale Akumva Oiŵala, 6/15

Musasiye Kuchita Zabwino, 8/15

Ndani Adzatisiyanitsa ndi Chikondi cha Mulungu? 10/15

“Ngati Mulungu Ali ndi Ife, Adzatikaniza Ndani?” 6/1

Onetsani Kuti Mukupita Patsogolo, 8/1

Opani Yehova ndi Kusunga Malamulo Ake, 12/1

Oyang’anira ndi Atumiki Otumikira Amaikidwa Mwateokalase, 1/15

Pezani Chimwemwe mwa Kukhala Wopatsa! 7/1

“Phunzirani kwa Ine,” 12/15

Samalirani Mzimu ndi Kukhala ndi Moyo! 3/15

Sangalalani Ndi Ntchito Yotuta! 7/15

Tamandani Yehova Chifukwa cha Ntchito Zake Zazikulu! 5/15

Taonani Wochita Zinthu Zodabwitsa! 4/15

Tchinjirizani Mtima Wanu, 10/15

Tsanzirani Yehova Pophunzitsa Ana Anu, 10/1

Tsiku la Yehova Lopereka Chiŵeruzo Layandikira! 2/15

‘Valani Kuleza Mtima,’ 11/1

Yehova Amatidziŵitsa Kuŵerenga Masiku Athu, 11/15

Yehova Ndi Mulungu Woleza Mtima, 11/1

Yehova Ndiye Pothaŵirapo Pathu, 11/15

Yenderani Limodzi ndi Gulu la Yehova, 1/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Ahasimoni, 6/15

Asikuti, 11/15

Chikhulupiriro cha Nowa Chimatsutsa Dziko Lapansi, 11/15

Chimwemwe, 3/1

Chitetezo M’dziko Loopsali, 2/1

Chokhalitsa Kuposa Golide, 8/1

Enoke Anayenda ndi Mulungu, 9/15

“Khalidwe Lobisika Lowononga Thanzi” (Zolaula za pa Intaneti), 4/15

Kodi Abambo a Tchalitchi Anachirikiza Choonadi cha Baibulo? 4/15

Kodi Chilipo Chimene Chingagwirizanitse Anthu? 9/15

Kodi Chofunika Kwambiri N’chiyani? 9/15

Kodi Mungakhulupirire Miyezo ya Ndani? 6/1

Kodi Mungapange Dziko Lapansi Kukhala Malo Abwinopo? 10/15

Kodi Munthu Akamwalira Amakhala ndi Moyo Kwinakwake? 7/15

Kukhulupirira Mizimu, 5/1

Kuona Ndalama M’njira Yoyenera, 6/15

Kuvutika, 5/15

Lamulo la Chikhalidwe Likugwirabe Ntchito, 12/1

Mabala a Nkhondo, 1/1

‘Mankhwala Opaka M’maso Mwanu!’ 12/15

Maziko a Zimene Mumakhulupirira, 8/1

Mdyerekezi, 9/1

Mitengo Imene Imakhalitsa, 7/1

“Mitsempha Yako Idzalandirapo Moyo,” 2/1

‘M’kuunika Kwanu Tidzaona Kuunika,’ 12/1

Mmene Mungapambanire Paunyamata Wanu, 8/15

Mutha Kukhala ndi Chikhulupiriro Chenicheni, 10/1

Mzimu Wosafa? 7/15

“Ndikachita Apilo kwa Kaisara!”

Opaleshoni Yopanda Magazi, 3/1

Origen​—Kodi Chiphunzitso Chake Chinakhudza Tchalitchi Motani? 7/15

Paradaiso Wauzimu, 3/1

Paulo Alinganiza Zopereka Zothandizira Oyera Mtima Pa Mavuto, 3/15

‘Taonani Khamu Lalikulu!’ 5/15

Uthenga Wabwino wa Ufumu, 4/1

Yamikirani Ndipo Sangalalani, 9/1

Zinthu Zowononga Mitengo, 11/1

Zomwe Tingaphunzire ku Mtengo wa Kanjedza, 10/1

OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA

2/1, 4/1, 5/1, 6/1, 8/1, 10/1, 12/1

YEHOVA

Limbikitsani Chikhulupiriro mwa Yehova, 6/1

“Madalitso a Yehova Alemeretsa,” 11/1

YESU KRISTU

Kodi Yesu Amapulumutsa Motani? 11/15

Kuuka, 3/15

Yesu Weniweni, 12/15