Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2003

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2003

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2003

Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo

BAIBULO

Anthu Wamba Anamasulira (Chitahiti), 7/1

Kulunjika Nawo Bwino Mawu a Choonadi, 1/1

MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA

Chifukwa chake manambala a mavesi m’buku la Masalmo amasiyana, 4/1

Chifuniro cha Mulungu chnachitika kale kumwamba? (Mat. 6:10), 12/15

Ezekieli anakhala wosalankhula? (Ezek. 24:27; 33:22), 12/1

Kubatizidwa chifukwa cha akufa (1 Akor. 15:29, KJ), 10/1

Kulumbira pofuna kunena zoona zokhazokha m’khoti? 1/15

Kumva mawu koma osaona amene akulankhula, ndiye kuti ziwanda n’zimene zikum’vutitsa, 5/1

“Magawo aŵiri” a mzimu wa Eliya (2 Maf. 2:9), 11/1

Mfundo ya mitala inasintha? 8/1

Miyala ya miyezi yobadwira, 11/15

“Mmodzi wa ife” (Gen. 3:22), 10/15

‘Moyo mwa Iye yekha’ (Yoh. 5:26; 6:53), 9/15

Mphatso za ukwati, 9/1

N’chifukwa chiyani munthu ayenera kufuula ngati wina akufuna kumugwirira? 2/1

N’kulakwa kupha galu kapena mphaka? 6/1

“Nthaŵi zonse” (1 Akor. 11:25, 26), 1/1

‘Onani Mlangizi,’ ‘Imvani mawu kumbuyo’ (Yes. 30:20, 21), 2/15

Pamene wodzozedwa yemwe akudwala sangathe kupezekapo pa Chikumbutso, 3/15

Satana ‘ali nayo mphamvu ya imfa’? (Aheb. 2:14), 7/1

Satana amatha kudziŵa zimene munthu akuganiza? 6/15

Ubatizo wa mu 33 C.E. unasonyeza kudzipatulira? 5/15

MBIRI YA MOYO WANGA

Anali Wokoma Mtima (M. Henschel), 8/15

Chimwemwe Chosayerekezeka! (R. Wallwork), 6/1

Kakalata Kamene Kanasintha Moyo Wanga (I. Hochstenbach), 1/1

Kufunafuna Ufumu Choyamba Ndiwo Moyo Wabwino ndi Wosangalatsa (J. Sunal), 3/1

Kuphunzitsidwa ndi Yehova Kuyambira pa Ubwana Wanga (R. Abrahamson), 11/1

Kutumikira Ena Kumachepetsa Mavuto (J. Arias), 7/1

Kuyesedwa mu Ng’anjo Yamoto (P. Yannouris), 2/1

“Ndidzabwezera Yehova Chiyani?” (M. Kerasinis), 12/1

Wodala Munthu Amene Mulungu Wake ndi Yehova (T. Didur), 8/1

Yehova Amakokera Anthu Odzichepetsa (A. Koshino), 10/1

Yehova Amatisamalira Nthaŵi Zonse (E. Mzanga), 9/1

Zimene Ndachitako pa Ntchito ya Padziko Lonse Yophunzitsa Baibulo (R. Nisbet), 4/1

MBONI ZA YEHOVA

Asanaphunzire ndi Ataphunzira, 1/15, 3/15, 5/15, 7/15, 9/15, 11/15

Atumiki a M’mayiko Ena (Dziko la Mexico), 5/1

Chizunzo, 3/1

Dziko la Brazil (gawo la osamva), 2/1

Dziko la Czech Republic, 8/1

Dziko la France, 12/1

Dziko la Poland, 10/1

Dziko la Ukraine, 10/1

Kalendala, 11/15

Khoti Lalikulu Lagamula Kuti Kulambira Koona Kupitirire (Dziko la Armenia), 4/1

Kukumbukira Amene Anaphedwa (Dziko la Hungary), 1/15

Kulalikira Kumakhaladi Kosaiŵalika (Dziko la Mexico), 4/15

Kulambira Koona Kugwirizanitsa Banja, 8/15

Kupindula Chifukwa cha Khama, 1/1

Kuthandizidwa Poonabe Magazi Kukhala Opatulika (Dziko la Philippines), 5/1

‘Linakwaniritsa Chimene Ndinkafuna Kwambiri’ (buku lakuti Yandikirani kwa Yehova), 7/1

Misonkhano ya “Olengeza Ufumu Achangu,” 1/15

Misonkhano ya “Patsani Mulungu Ulemerero,” 3/1

Mmene Anthu Amakhalira pa Msasa wa Anthu Othaŵa Kwawo (Dziko la Tanzania), 2/15

“Moyo Ndi Wokoma!” 1/1

Mwambo Womaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15

Ogwiritsa Ntchito Chinenero Chapadera (Dziko la Korea), 6/15

“Okonzeka pa Ntchito Iliyonse Yabwino,” 12/1

São Tomé ndi Príncipe, 10/15

Vidiyo Imene Imakhudza Mitima ya Achinyamata, 7/1

MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU

Achinyamata, Yendani Moyenera Yehova, 10/15

Achinyamatanu Mukupita Patsogolo Mwauzimu? 4/1

Chikondi, 7/1

Ganizani Bwino Kuti Muchite Zinthu Mwanzeru, 7/15

Khalani ndi Mtima Wopatsa, 11/1

Khalani Okhazikika, 5/15

Kuchita Zinthu Moganizira Ena, 8/1

Kufuna Yehova Mwakhama, 8/15

Kugwiritsira Ntchito Bwino Kusintha kwa Zinthu, 3/1

Kukwanitsidwa ndi Zimene Tili Nazo, 6/1

Kumvetsa Cholinga cha Kulanga, 10/1

Kuona Kuti Okhulupirira Achikulire ndi Ofunika Kwambiri, 9/1

Kupatsa Kumene Kumasangalatsa Mulungu, 6/1

“Limbikani, Ine Ndaligonjetsa Dziko Lapansi,” 3/15

“Malamulo A Wanzeru” (Miy. 13), 9/15

‘Milomo ya Ntheradi’ (Miy. 12), 3/15

‘Mulungu Akomera Mtima Wabwino’ (Miy. 12), 1/15

Mumafunikira Lamulo la M’Baibulo Nthaŵi Zonse? 12/1

“Munalandira Kwaulere, Patsani Kwaulere,” 8/1

‘Musakhale Womangidwa m’Goli ndi Wosiyana,’ 10/15

Musalekerere Mtima wa Mwana Wanu! 2/15

Mwana Wanga Azipita ku Sukulu? 3/15

Tamandani Yehova ‘Pakati pa Msonkhano,’ 9/1

Yehova Amaona Zimene Inu Mumachita? 5/1

NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA

Achinyamata Amene Amakondweretsa Mtima wa Yehova, 4/15

Achinyamatanu​—Yehova Sadzaiŵala Ntchito Yanu! 4/15

Akazi Achikristu Okhulupirika Ndi Olambira Mulungu Ofunika Kwambiri, 11/1

Akazi Amene Anakondweretsa Mtima wa Yehova, 11/1

Atumiki a Yehova Ali ndi Chiyembekezo Chenicheni (Mika), 8/15

Chitonthozo Chenicheni Chingapezeke Kuti? 5/1

Dalirani Yehova, 9/1

“Dikirani”! 1/1

Imani ndi Kupenya Chipulumutso cha Yehova! 6/1

‘Khalani Amphamvu Ndipo Limbikani Mtima!’ 3/1

Khalani Maso Kuposa Kale Lonse! 1/1

Khalani Okonzekeratu Tsiku la Yehova, 12/15

“Khalani Oyamikira,” 12/1

Khalani Wodziletsa Kuti Mudzalandire Mphoto! 10/15

‘Khalanibe M’mawu Anga,’ 2/1

Khulupirirani Yehova ndi Mtima Wanu Wonse, 3/1

Khulupirirani Yehova Panthaŵi za Mavuto, 9/1

Kodi Chikhulupiriro Chanu N’cholimba Bwanji? 1/15

Kodi Muli ndi Mtima Wodikira? 7/15

Kodi Mumakhulupiriradi Uthenga Wabwino? 1/15

Kodi Yehova Amafuna Chiyani kwa Ife? (Mika), 8/15

‘Kondanani Wina ndi Mnzake,’ 2/1

“Kondwerani mwa Yehova,” 12/1

Kristu Akulankhula ku Mipingo, 5/15

Kufatsa Ndi Khalidwe Lachikristu Lofunika Kwambiri, 4/1

Kukambirana Nkhani Zauzimu Kumalimbikitsa, 9/15

Kupirira Poyesedwa Kumalemekeza Yehova, 10/1

Kutsanzira Mulungu wa Choonadi, 8/1

Kuzunzika Chifukwa cha Chilungamo, 10/1

Lalikirani ndi Cholinga Chopanga Ophunzira, 11/15

‘Lunjikani Nawo Bwino Mawu a Mulungu,’ 11/15

Mgonero wa Ambuye Uli ndi Phindu Lanji kwa Inu? 2/15

Mmene Akristu Oyambirira Anachitira ndi Chilamulo cha Mose, 3/15

“Mubale Chipatso Chambiri,” 2/1

“Mulungu Ndiye Chikondi,” 7/1

Mumafunsa Kuti, “Ali Kuti Yehova?” 5/1

“Musaope, Kapena Kutenga Nkhaŵa,” 6/1

Muziyang’ana Ubwino wa Onse, 6/15

Mverani Zimene Mzimu Ukunena! 5/15

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuchita Chikumbutso cha Mgonero wa Ambuye? 2/15

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera Kosaleka? 9/15

Onani Ena Monga Momwe Yehova Amawaonera, 3/15

Onetsani ‘Kufatsa Konse pa Anthu Onse,’ 4/1

“Taonani, Uyu Ndiye Mulungu Wathu,” 7/1

Thandizani Ena Kulabadira Uthenga wa Ufumu, 11/15

Tidzayenda M’dzina la Yehova Mpaka Muyaya! (Mika), 8/15

Tifunika Kukhala Maso Kwambiri Tsopano, 12/15

Tiziwaona Bwanji Anthu Pamene Tsiku la Yehova Likuyandikira? 7/15

Tonthozani Amene Ali ndi Chisoni, 5/1

Tsanzirani Yehova, Mulungu Wathu Wopanda Tsankho, 6/15

Wonjezerani Kudziletsa pa Chizindikiritso Chanu, 10/15

Yehova, Mulungu wa Choonadi, 8/1

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Alexander VI (papa), 6/15

Anafunafuna Njira Yochepetsetsa (Mgwirizano wa Abale), 12/15

Baibulo Lingathandize Ukwati, 9/15

Baraki, 11/15

Chifukwa chake Mulungu Amalola Mavuto, 1/1

Chikumbutso (Mgonero wa Ambuye), 4/1

Dziko la Paradaiso, 11/15

Eusebius​—Kodi Anali “Woyamba Kulemba Mbiri ya Tchalitchi”? 7/15

Guwa la Nsembe N’lofunika Polambira? 2/15

‘Khalani ndi Chikumbumtima Chabwino,’ 5/1

Kodi Mphamvu Zoipa Zapambana? 1/15

Kodi Timafunikadi Anthu Ena? 7/15

Kufukiza, 6/1

Kukoma Mtima Kwachikondi, 4/15

Kuona Mtima, 2/1

Kusangalala Ndiponso Kukhalitsa pa Ntchito, 2/1

Kusankha Zochita, 10/15

Kuthandiza Osoŵa, 6/1

‘Kutsalima Pachothwikira’ (Mac. 26:14), 10/1

Maganizo Abwino pa Nkhani ya Ntchito, 2/1

Martin Luther, 9/15

Mkuyu, 5/15

Moyo Wauzimu, 4/15

‘Mpingo Woona’ Umodzi Wokha? 9/1

Mukufuna Kuti Anthu Adzakukumbukireni Ngati Munthu Wotani? 8/15

N’chiyani Chinaichitikira? (Nofi ndi No), 7/1

Ndani Tingamukhulupirire? 11/1

Nkhani ya Nowa, 5/15

‘Solomo Sanavala Monga Limodzi la Ameneŵa,’ 6/1

Tatian Anali Woikira Kumbuyo Chikristu Kapena Anali Wopanduka? 5/15

Thandizo kwa Anthu Osauka, 9/1

Ugariti​—Mzinda Wakale, 7/15

Ukwati wa Boazi ndi Rute, 4/15

Umphaŵi, 3/15, 8/1

Yakobo, 10/15

Zimene Mbalame Zingatiphunzitse, 6/15

Zitsime, 12/1

YEHOVA

Amaganizira Anthu Wamba, 4/15

Amaganiziradi Anthu? 10/1

Amaona Zimene Inu Mumachita? 5/1

Chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhulupirira Mulungu? 12/1

Mafunso Ofunika Kufunsa Mulungu, 5/1

Wofunika Kum’dziŵa, 2/15

YESU KRISTU

Anakhalako Padziko Lapansi? 6/15

Makolo ndi Achibale, 12/15