Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalozera wa Nkhani za M’magazini a Nsanja ya Olonda a 2006

Kalozera wa Nkhani za M’magazini a Nsanja ya Olonda a 2006

Kalozera wa Nkhani za M’magazini a Nsanja ya Olonda a 2006

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

BAIBULO

Anachita Khama Polimbikitsa (Seraphim), 5/15

Christophe Plantin​—Ntchito Yosindikiza Mabaibulo, 11/15

“Ha! Ndikondadi Chilamulo Chanu,” 9/15

Kodi Lili ndi Malamulo Okhwima Kwambiri? 10/1

Kumvetsa Baibulo, 4/1

Mabuku a M’Baibulo (mpukutu wa Muratori), 2/15

“Mawu Akale Kwambiri Otengedwa M’Baibulo,” 1/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Ezara, 1/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Nehemiya, 2/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Estere, 3/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Yobu, 3/15

Mfundo Zazikulu za Chigawo Choyamba cha Masalmo, 5/15

Mfundo Zazikulu za Chigawo Chachiwiri cha Masalmo, 6/1

Mfundo Zazikulu za Chigawo Chachitatu ndi Chachinayi cha Masalmo, 7/15

Mfundo Zazikulu za Chigawo Chachisanu cha Masalmo, 9/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Miyambo, 9/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Mlaliki, 11/1

Mfundo Zazikulu za Nyimbo ya Solomo, 11/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Yesaya​—Gawo 1, 12/1

“Tiyerekezere Lemba ndi Lemba Linzake,” 8/15

KALENDALA

Kuchitira Umboni “Molimba Mtima,” 11/15

Kuwomboledwa ndi ‘Mwazi wa Mtengo Wapatali,’ 3/15

‘Mulungu Wathu Akhoza Kutilanditsa’ (Ahebri atatu), 7/15

‘Sitingaleke Kulankhula,’ 9/15

“Yehova Ndiye Mwini Nkhondo,” 5/15

‘Yehova Wakhala Chipulumutso Changa,’ 1/15

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

Chiyeso chomaliza chikadzatha, kodi anthu adzachimwa ndi kufa? 8/15

Kodi akazi ayenera kukhala “chete” mumpingo? (1 Ak. 14:34), 3/1

Kodi dziko lapansili lidzawonongedwa? (Sl 102:26), 1/1

Kodi Mose “sadzaloledwanso kutuluka”? (De 31:2), 10/1

Kodi munthu angachotsedwe chifukwa chochita chidetso? 7/15

Kodi “nzeru imanena za Yesu Khristu asanabadwe padziko monga munthu? (Miy 8), 8/1

Kodi Yesu analankhula mopanda ulemu kwa mayi ake? (Yoh 2:4), 12/1

Kodi Yosefe anawombeza maula? (Ge 44:5), 2/1

“Kulibe munthu anakwera Kumwamba, koma Iye wotsikayo,” (Yoh 3:13), 6/15

N’chifukwa chiyani m’Chilamulo cha Mose zinthu zachibadwa zokhudza kugonana ndi kubereka zinadetsa munthu? 6/1

N’chiyani chikuchititsa kuti “zofunika” zifike? (Hag 2:7), 5/15

Ngozi yagalimoto yomwe anthu afapo, 9/15

“Usaphike mwana wa mbuzi mu mkaka wa make” (Eks 23:19), 4/1

Zimene zinali mu likasa lachipangano, 1/15

Zinthu zoopsa zitatu ziti? (Mt 5:22), 2/15

Ziwandazo zisiye kuvutitsa, 4/15

MBIRI YA MOYO WANGA

Banja Linagwirizana Patatha Zaka Zambiri (S. Hirano), 8/1

Kudziwa Chifukwa Chimene Mulungu Amalolera Anthu Kuvutika (H. Peloyan), 5/1

Kudziwa ndi Kuchita Chabwino (H. Sanderson), 3/1

Kukhulupirika kwa Achibale Anga Kwandithandiza (K. Cooke), 9/1

Kukondwera ndi Chilamulo cha Yehova (A. Schroeder), 9/15

Kulera ana Eyiti (J. Valentine), 1/1

Kupirira Kumabweretsa Chimwemwe (M. Rocha de Souza), 7/1

Ndikudwala Koma Ndikutumikira Yehova Mwachimwemwe (V. Spetsiotis), 6/1

Otsimikiza Kutumikira Yehova (R. Kuokkanen), 4/1

Tinayesetsa Kuti Tikhalebe Olimba Mwauzimu (R. Brüggemeier), 12/1

Yehova Anadalitsa Mtima Wofuna Kukhala Mmishonale (S. Winfield da Conceição), 11/1

Yehova Anandithandiza Kum’peza (F. Clark), 2/1

Yehova Anandithandiza Kupirira Mavuto pa Moyo (D. Irwin), 10/1

MBONI ZA YEHOVA

Abale Atsopano a M’Bungwe Lolamulira, 3/15

“Chifukwa cha Mwana wa Zaka Naini,” 9/1

Chikhulupiriro Chimalimbikitsa Ena (zilumba za Canary), 7/1

Daniel ndi Baji Yake ya Msonkhano, 11/1

Guinea, 10/15

Haiti, 12/15

Kansalu Kapepo, 2/15

Kodi Woweruza Angalangizidwe? 12/1

Kumanga Mogwirizana, 11/1

Kuyamba N’kuthamangitsidwa, Kenako Kukondedwa (Peru), 1/1

‘Kuyambira Lero, Ndakhulupirira Kuti Kuli Mulungu’ (Czech Republic), 7/15

Matawuni Aang’ono ku Bolivia, 2/15

Misonkhano Yakuti “Chipulumutso Chayandikira,” 3/1

Mwambo Womaliza Maphunziro a Gileadi, 1/1, 7/1

“Njira Yabwino” (Spain), 7/1

Ntchito Ikupita Patsogolo (Taiwan), 8/15

Panama, 4/15

Phunzitsani Ana Anu Kupereka Ndemanga, 11/15

Sukulu Yophunzitsa Utumiki, 11/15

“Tapitiriza!” (mwana wa sukulu ku Russia), 3/1

Uganda, 6/15

Ulendo Unasintha Maganizo Ake, 7/1

Wokalamba Koma Wosasungulumwa (F. Rivarol), 8/15

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKRISTU

Chilimbikitso kwa Okalamba, 6/1

Chuma Chenicheni, 2/1

Ikapita Sibweranso, Igwiritseni Ntchito Bwino (nthawi), 8/1

Kuganizira Osauka, 5/1

Kulankhulana ndi Mwamuna Kapena Mkazi Wanu, 4/15

Kulera Ana, 11/1

Kuona Mtima N’kopindulitsa, 12/1

Kuopa Mulungu “Ndiko Mwambo Wanzeru” (Miy 15), 8/1

Kuphunzitsa Mwana Momugwira Mtima, 5/1

Kusankha Zinthu Mokondweretsa Mulungu, 4/15

Kutumikira Mumpingo wa Chinenero China, 3/15

Makolo, Khalani Chitsanzo Chabwino, 4/1

“Mawu a pa Nthawi Yake,” 1/1

Mtengo wa “Chotengera Chochepa Mphamvu,” 5/15

Musaope, 5/1

Muzisangalala Nako Kusinkhasinkha, 1/1

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuchita Zabwino? 11/15

Nkhani Imene Ikukukhudzani, 11/15

Phunziro Lonena za Kunyada ndi Kudzichepetsa, 6/15

Tsanzirani Khristu Mukamalamulira Ena, 4/1

Tsatirani Mfundo za M’Baibulo Kuti Mupeze Chimwemwe, 6/1

Tsiku la Ukwati, 10/15

“Ufulu wa Kulankhula,” 5/15

Wachibale Akasiya Yehova, 9/1

“Wosamalira Chidzudzulo Amachenjera” (Miy 15), 7/1

NKHANI ZOPHUNZIRA

Abusa Omwe Ndi ‘Zitsanzo kwa Gulu’ la Nkhosa, 5/1

Achinyamata, Sankhani Kutumikira Yehova, 7/1

Anabadwira mu Mtundu Wosankhika wa Mulungu, 7/1

Ganizirani za Ubwino wa Gulu la Yehova, 7/15

“Ha! Ndikondadi Chilamulo Chanu,” 6/15

“Ine Ndili Nanu,” 4/15

Kanizani Satana, Ndipo Iye Adzathawa! 1/15

Khalani Anzeru mwa Kuopa Mulungu, 8/1

Khalanibe M’chikondi cha Mulungu, 11/15

Kodi Chikhulupiriro Chanu mwa Mulungu N’cholimba Motani? 1/1

Kodi Mumaona Zinthu Zopatulika Monga Mmene Yehova Amazionera? 11/1

Kodi Mwakonzekera Kupulumuka? 5/15

Kodi Zochita Zanu Zimatsimikizira Kuti Muli ndi Chikhulupiriro? 10/15

Kondani Mulungu Amene Amakukondani, 12/1

Kufunafuna Chilungamo Kungatiteteze, 1/1

Kukwaniritsa Zimene Zimafunika Paubatizo Wachikhristu, 4/1

Kulemekeza Misonkhano Yathu Yopatulika, 11/1

Kulimba Mtima Chifukwa cha Chikhulupiriro ndi Kuopa Mulungu, 10/1

Kulimba Mtima Kwambiri Chifukwa cha Chikondi, 10/1

Kusonkhanitsa Zinthu za Kumwamba ndi za Padziko Lapansi, 2/15

Kutumikira Khristu Mfumu Mokhulupirika, 5/1

Kuyenda M’njira ya Kuunika Komawalabe, 2/15

Landirani Chilango cha Yehova Nthawi Zonse, 11/15

Makonzedwe Okwaniritsira Cholinga cha Mulungu, 2/15

Manja Anu Alimbike, 4/15

Mmene Tingam’fikire “Wakumva Pemphero,” 9/1

“Mudamva za Chipiriro cha Yobu,” 8/15

Musam’patse Malo Mdyerekezi, 1/15

Muziganiza Bwino Kwambiri, 3/1

Opani Yehova Kuti Mukhale Achimwemwe, 8/1

Pewani Kudandaula, 7/15

Pewani Kulambira Konyenga! 3/15

Pitani Mukapange Ophunzira, ndi Kuwabatiza, 4/1

“Sankhani Moyo Kuti Mukhale ndi Moyo,” 6/1

Sonyezani Chikondi ndi Ulemu mwa Kulamulira Lilime Lanu, 9/15

Tanthauzo la Kukonda Mnansi Wathu, 12/1

Tsanzirani Kuleza Mtima kwa Yehova, 2/1

“Tsiku Lalikulu la Yehova Lili Pafupi,” 12/15

Ubwino Woyenda Mwangwiro, 5/15

‘Ukondwere ndi Mkazi Wokula Naye,’ 9/15

Ukwati Wolemekezeka kwa Mulungu ndi kwa Anthu, 10/15

‘Umboni kwa Anthu a Mitundu Yonse,’ 2/1

Yehova Adzaonetsetsa Kuti “Chilungamo Chachitika,” 12/15

Yehova Amalalikira ‘za Chimaliziro Kuchokera Pachiyambi,’ 6/1

Yehova Amalanditsa Wovutika, 7/15

Yehova Amapereka “Mzimu Woyera kwa Amene Akum’pempha,” 12/15

Yehova Amaphunzitsa Abusa a Nkhosa Zake, 5/1

Yembekezani Yehova Kuti Mukhale Olimba Mtima, 10/1

“Yense Adzasenza Katundu Wake wa Iye Mwini,” 3/15

Yobu Anali Munthu Wopirira ndi Wosunga Umphumphu, 8/15

‘Zikumbutso Zanu Ndizo Zondikondweretsa,’ 6/15

“Zopempha Zanu Zidziwike kwa Mulungu,” 9/1

Zosangalatsa Zomwe Zimatsitsimula, 3/1

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Angelo, 1/15

Baruki, Mlembi wa Yeremiya, 8/15

Bwalo la Akulu, 9/15

Chidindo cha Yukali, 9/15

Chimwemwe, 6/15

Choonadi Chenicheni, 7/1

Chuma ndi Khalidwe, 2/1

Kayendedwe Panyanja Yaikulu, 10/1

Khirisimasi, 12/15

Kodi Chabwino Chidzagonjetsa Choipa? 1/1

Kodi Mukufuna Kukhala ndi Anzanu Enieni? 3/1

Kodi Tikukhala ‘M’masiku Otsiriza’? 9/15

Kodi TV Ndi Njira Yabwino Yolerera Ana? 6/15

Kodi Yuda Anakhaladi Bwinja? 11/15

Kodi Zipembedzo Zili ndi Phindu Lanji? 9/1

Kukhala ndi Moyo Wosatha, 10/1

Kupatsidwa Ulemu, 8/1

Kupembedza Komwe Kungapindulitse, 9/1

Malaya Aubweya, 8/1

Melito wa ku Sarde, 4/15

Misewu ya Aroma, 10/15

Mtendere Padziko Lapansi, Kodi N’kulota? 12/15

Mtengo wa Lagani Auna, 2/1

“Mudzi Woposa Midzi Yonse M’Galileya” (Sepphoris), 6/1

Mwala Wosema Umatchula za Isiraeli, 7/15

Mwambo Wosamba wa Ayuda, 10/15

Mzinda wa Ebla Wapezekanso, 12/15

“N’chifukwa Chiyani Tili ndi Moyo?” 10/15

Ndani Adzalandire Dziko Lapansi? 8/15

Njira Yothetsera Imfa, 3/15

Nkhani ‘Yophiphiritsira,’ 3/15

Samalirani “Mpesa Uwu”! 6/15

Ufumu wa Mulungu, 7/15

Umphawi, 5/1

Wokana Khristu, 12/1

Zinyama Zimalemekeza Yehova, 1/15

YEHOVA

Cholinga cha Dziko Lapansili, 5/15

Kodi Tingam’dziwedi Mulungu? 10/15

Ufulu Wokhala ndi Dzina, 4/15

YESU KRISTU

Kodi Ndani Akutsatira Ziphunzitso za Khristu? 3/1

Kubwera kwa Mesiya, 2/15

Mkulu wa Ansembe Amene Anaphetsa Yesu, 1/15