Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mungafune Kukuchezerani?

Kodi Mungafune Kukuchezerani?

Kodi Mungafune Kukuchezerani?

Ngakhale m’dziko lamavutoli, mungakhalebe osangalala podziwa zenizeni zimene Baibulo limaphunzitsa pa nkhani ya Mulungu, Ufumu wake, ndi cholinga chimene iye ali nacho chakuti anthu adzakhale ndi moyo wabwino kwambiri. Ngati mukufuna kudziwa zambiri kapena kuti wina aziphunzira nanu Baibulo panyumba panu kwaulere, lembani kalata n’kuitumiza kwa Mboni za Yehova, P.O. Box 30749, Lilongwe 3, kapena gwiritsani ntchito adiresi yoyenerera pa maadiresi amene ali patsamba 2.