Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

January 15, 2008

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:

February 11-17, 2008

Onetsetsani Kuti Mukusamala Utumiki Umene Munaulandira mwa Ambuye

TSAMBA 4

NYIMBO ZOIMBA:: 193, 151

February 18-24, 2008

Yang’anirani ‘Luso Lanu la Kuphunzitsa’

TSAMBA 8

NYIMBO ZOIMBA:: 6, 123

February 25, 2008–March 2, 2008

Anthu Amene Ali ndi “Maganizo Oyenerera” Akulabadira

TSAMBA 13

NYIMBO ZOIMBA:: 156, 133

March 3-9, 2008

Oyenerera Kulandira Ufumu

TSAMBA 20

NYIMBO ZOIMBA:: 195, 60

March 10-16, 2008

Oyenerera Kutsogoleredwa ku Akasupe a Madzi a Moyo

TSAMBA 24

NYIMBO ZOIMBA:: 99, 187

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1-3 MASAMBA 4-​17

Nkhani zophunzira zitatuzi zikulimbikitsani kuti musasiye kuchita utumiki wachikhristu. Zikukumbutsani chifukwa chake muyenera kukhala achangu, zikusonyezani mmene mungakulitsire ‘luso lanu la kuphunzitsa,’ ndipo zikulimbikitsani pokusonyezani kuti anthu ambiri akulabadirabe ntchito yolalikira.

Nkhani Zophunzira 4, 5 MASAMBA 20-​28

Nkhani ziwirizi zikufotokoza mwatsatanetsatane chiyembekezo chimene Akhristu oona ali nacho. Kaya mukuyembekezera kukakhala ndi Khristu kumwamba kapena kukhala ndi moyo wosatha padziko lapansi muulamuliro wa Ufumu wa Mulungu, zikuthandizani kumvetsa ndi kuyamikira kukoma mtima kwa Yehova ndi nzeru zake zosasanthulika.

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Magazini Yophunzira Yatsopano ya Nsanja ya Olonda

TSAMBA 3

Moyo Wawo Unakhala Waphindu​—Nanga Inuyo Bwanji?

TSAMBA 17

Mawu a Yehova Ndi Amoyo​—Mfundo Zazikulu za M’buku la Mateyo

TSAMBA 29

Akhristu Akamapetedwa Ngati Tirigu

TSAMBA 32